score
float32
1.04
1.25
Chichewa
stringlengths
10
497
Tigrinya
stringlengths
10
498
1.249439
Mungatowezera cikhulupiro ca Nowa, munakwanisambo kupulumusa umaso wanu na wa ale anafuna imwe.
ኣስኣሰር እምነት ኖህ እንተ ስዒብካ፡ ንስኻ እውን ንርእስኻን ነቶም እትፈትዎምን ከተድሕን ትኽእል ኢኻ።
1.249424
46 Penepo, mbuya wace anadza kabwera ntsiku ikhakhonda iye kudikhira, pa n'dzidzi unakhonda iye kudziwa.
ጐይታ እቲ ባርያ እቲ፡ ንሱ ብዘይተጸበያ መዓልቲ ብዘይፈላጣ ጊዜውን ኪመጽእ እዩ።
1.247489
Ndinu kulima Mulungu; ndinu yomanga Mulungu.
ንስኻትኩም ሕርሻ ኣምላኽ፡ ህንጻ ኣምላኽ ኢኹም።
1.247311
64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira."
64 ገለ ኻባኻትኩም ግና ዘይኣምኑ ኣለዉ" በሎም።
1.246644
Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa."
ሓንቲ እኳ ኻብኣተን ብዘይ ፍቓድ ሰማያዊ ኣቦኹም ኣብ ምድሪ ኣይትወድቕን እያ።
1.246618
9Iye sanasiyanitse pakati pa ife ndi iwo, pakuti anayeretsa mitima yawo mwachikhulupiriro.
9ልቦም ብእምነት ስለ ዘንጽሀ ኣብ መንጎናን ኣብ መንጎኣቶምን ሓንቲ እኳ ኣይፈላለየን።
1.246501
M'malomwake ananena kuti: "Kudwala kumeneku si kwa imfa chabe, koma n'kopatsa Mulungu ulemerero, kuti mwa kudwalako, Mwana wa Mulungu alemekezeke."
የግዳስ፡ "እዚ ሕማም እዚ፡ ወዲ ኣምላኽ ብእኡ ምእንቲ ኪኸብር፡ ንኽብሪ ኣምላኽ እዩ እምበር፡ ንሞት ኣይኰነን" በለ።
1.246326
Ngati nanunso mutatsanzira chikhulupiriro cha Nowa, zingathandize kuti inuyo ndi banja lanu mudzapulumuke.
ኣስኣሰር እምነት ኖህ እንተ ስዒብካ፡ ንስኻ እውን ንርእስኻን ነቶም እትፈትዎምን ከተድሕን ትኽእል ኢኻ።
1.24526
Musamaope munthu aliyense, pakuti chiweruzo ndi cha Mulungu.
ፍርዲ ናይ ኣምላኽ እዩ እሞ፡ ገጽ ሰብ ኣይትፍርሁ።
1.244964
Ngati nanunso mutatsanzira chikhulupiriro cha Nowa, zingathandize kuti inuyo komanso banja lanu mudzapulumuke.
ኣስኣሰር እምነት ኖህ እንተ ስዒብካ፡ ንስኻ እውን ንርእስኻን ነቶም እትፈትዎምን ከተድሕን ትኽእል ኢኻ።
1.244627
Ngakhale atakuchimwirani kasanu ndi kawiri patsiku ndipo abwereranso kwa inu maulendo asanu ndi awiri nati, 'Ndalapa,' muyenera kuwakhululukira.
ኣብ መዓልቲ ሸውዓተ ሳዕ እኳ እንተ በደለካ፡ 'ተጣዒሰ' እናበለ ኸኣ ሸውዓተ ሳዕ ናባኻ እንተ ተመሊሱ፡ ሕደገሉ።
1.243392
Tsopano ife tikudziwa kuti chiweruzo cha Mulungu, chotsutsa amene amachita zinthu zotere, nʼchokhazikika pa choonadi.
"ንሕናስ ኣብቶም ከምዚ ዝበለ ዚገብሩ እቲ ፍርዲ ኣምላኽ ሓቂ ምዃኑ ንፈልጥ ኢና።
1.242349
35 Ndipo iye adati kwa iwo, amuna inu a Israyeli, tamachenjerani mwa inunokha za anthu awa, chimene muti muwachitire.
35 በሎም ድማ፡ኣቱም ሰብ እስራኤል፡ ኣብዞም ሰባት እዚኣቶም ክትገብርዎ እትሐስብዎ ዘሎኸም ተጠንቀቑሉ።
1.242081
44 Koma iwo adaganiza kuti Iye adali m'chipilingu cha ulendo, nayenda ulendo wa tsiku limodzi; ndipo adayamba kumfunafuna Iye mwa abale awo ndi mwa anansi awo.
ምስ ሰብ መገዲ ዘሎ መሲልዎም፡ መገዲ ሓንቲ መዓልቲ ኸዱ፡ ኣብ ኣዝማዶምን ኣብ ዚፈልጥዎምን ከኣ ደለይዎ።
1.241795
15Anati kwa iwo, "Pitani mʼdziko lonse lapansi ndipo mukalalikire Uthenga Wabwino kwa zolengedwa zonse.
15 ከምዚ ድማ በሎም፦ "ናብ ኵላ ዓለም ኪዱ፡ ንዅሉ ፍጥረት ከኣ ብስራት ስበኹሉ።
1.241614
4 Ngakhale akuchimwire maulendo 7 pa tsiku, n'kubwera kwa iwe maulendo 7, kudzanena kuti, 'Ndalapa ine,' umukhululukire ndithu."+
ኣብ መዓልቲ ሸውዓተ ሳዕ እኳ እንተ በደለካ፡ 'ተጣዒሰ' እናበለ ኸኣ ሸውዓተ ሳዕ ናባኻ እንተ ተመሊሱ፡ ሕደገሉ።
1.241266
Koma anapulumutsa Loti wolungamayo, amene anavutika mtima kwambiri ndi anthu ophwanya malamulo, mwa kulowerera kwawo khalidwe lotayirira."
ነቲ ብኣበሳኦምን ብርኹስ ንብረቶምን ዚስቀ ዝነበረ ሎጥ ጻድቕ ግና ኣድሐኖ፡
1.240969
Umenewu ndi ubwino wa Allah; amaupereka kwa amene wamfuna.
ንዘደለዮ ልዕል ኣበሎ፣ ንዝደለዮ ኸኣ ኣዋረዶ።
1.240178
Ngakhale atakuchimwirani kasanu ndi kawiri pa tsiku, ndikubwereranso maulendo asanu ndi awiri nkunena kuti, 'Ndalapa,' muyenera kuwakhululukira. "
ኣብ መዓልቲ ሸውዓተ ሳዕ እኳ እንተ በደለካ፡ 'ተጣዒሰ' እናበለ ኸኣ ሸውዓተ ሳዕ ናባኻ እንተ ተመሊሱ፡ ሕደገሉ።
1.240148
Mpostolo Juwau adanemba kuti: 'Ule omwe an'khulupira Mwanayo ana moyo wakusaya kumala, omwe an'khulupira lini Mwanayo an'dzaugumana lini moyo, koma ukali bwa Mulungu bun'dzakhala pa iye.'
ሃዋርያ ዮሃንስ፡ "እቲ ብወዲ ዚኣምን፡ ናይ ዘለኣለም ህይወት ኣላቶ፣ እቲ ንወዲ ዘይእዘዞ ግና፡ ቍጥዓ ኣምላኽ ደኣ ኣብኡ ይነብር እምበር፡ ንህይወት ኣይኪርእያን እዩ" ኢሉ ጸሓፈ።
1.239902
Kenako ananena kuti: "Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse."
ሽዑ ድማ፡ 'ኪዱ ኻብ ኵሎም ኣህዛብ ደቀ መዛሙርቲ ግበሩ።
1.239586
Allah ndiye Wamkulu kuposa iwo amunawo.
ኣምላኽ ካብ መዋቲ ሰብ ኣጸቢቑ ይዓቢ እዩ።
1.239152
Limati: "Yehova ali pafupi ndi onse oitanira pa iye.
"የሆዋ ንዅሎም እቶም ዚጽውዕዎ፡ ንዅሎም እቶም ብሓቂ ዚጽውዕዎ ቐረባኦም እዩ።
1.237798
Ngakhale anthu amene amapita kutchalitchi sadziwa bwinobwino Malemba.
መብዛሕትኦም እቶም ሃይማኖተኛታት ዚብሃሉ እውን እንተ ዀኑ፡ ብዛዕባ ቕዱሳት ጽሑፋት ሒደት ፍልጠት እዩ ዘለዎም።
1.237533
January 2013 _ Kodi Muyenera Kuopa Kutha kwa Dzikoli?
ጥሪ 2013 መወዳእታ ዓለም ኬፍርሃካ ይግባእዶ፧
1.237508
5 Farao anati kwa Yosefe, "Abambo ako ndi abale ako abwera kwa iwe.
5 ፈርኦን ድማ ንዮሴፍ፤ ኣቦኻን ኣሕዋትካን መጺኦምኻ።
1.237334
Pakuti anthu wochimwa amachitanso chomwecho.
ከምኡስ ኃጥኣንውን ይገብሩ እዮም።
1.237263
Khalani Wokhululuka 131.
ይቕረ በሃልቲ ንኹን 131.
1.237217
Anapita nawo kumpoto ndi kum'mawa.
ናብ ሰሜንን ናብ ምብራቕን ተወስዱ
1.235383
Popeza iwo asankha njira zawozawo,
መገድታት ርእሶም ሓርዮም፣
1.235067
maso ali nawo, koma sapenya;
ኣዒንቲ ኣለዎም፡ ግናኸ ኣይርእዩን፣
1.234795
Iye adzakhala wamkulu ndipo adzatchedwa Mwana wa Wammwambamwamba.
ንሱ ዓብዪ ኪኸውን፡ ወዲ እቲ ልዑል እውን ኪብሃል እዩ፣ .
1.234284
Mtumwi Paulo ananenanso kuti "olungama ndi osalungama omwe" adzaukitsidwa.
ሃዋርያ ጳውሎስ እውን፡ "ንጻድቃንን ንሓጥኣንን" ትንሳኤ ኸም ዚኸውን ገሊጹ ኣሎ።
1.234089
Mwina mumpingo wanu muli m'bale amene zochita kapena zolankhula zake sizimakusangalatsani.
ምናልባት ብዘረባኡን ብተግባራቱን ቅጭ ዜምጽኣልካ ሓው ኣብ ጉባኤኻ ይህሉ ይኸውን።
1.233455
Komano zikugwirizana bwanji ndi nkhani yokhudza Ufumu wa Mulungu komanso chaka cha 1914?
ግናኸ እዚ ምስ መንግስቲ ኣምላኽ ኰነ ምስ 1914 እንታይ ርክብ ኣለዎ፧
1.233444
14 Makolo achikhristu amafunikanso kulimba mtima.
14 ክርስትያን ወለዲ እውን ትብዓት የድልዮም እዩ።
1.233287
Yesu ananenanso kuti: "Ndili ndi zambiri zakuti ndikuuzeni, koma padakali pano simungathe kuzimvetsa zonsezo."
የሱስ ቀጺሉ፡ "ገና ብዙሕ ዝነግረኩም ኣሎኒ፣ ግናኸ፡ ሕጂ ኽትጾርዎ ኣይትኽእሉን ኢኹም" በሎም።
1.232467
Popeza Mulungu ndi wamuyaya, zaka 1,000 zili ngati tsiku limodzi kwa iye.
ኣምላኽ ዘለኣለማዊ ስለ ዝዀነ፡ ሽሕ ዓመት ንዕኡ ልክዕ ከም ሓንቲ መዓልቲ እዩ።
1.232137
(ndikuyamba) m'dzina la Allah, kuyamikidwa konse ndi kwa Allah.
ብስም ኣላህ እቲ ፍጹም ርህሩህ እቲ ኣዝዩ ራህራሂ
1.232039
Ngati mutaganizira zimene Mulungu wachitira anthu onse komanso inuyo panokha, n'zoonekeratu kuti watichitira zinthu zambirimbiri.
ብዛዕባ እቲ ኣምላኽ ንዓኻን ንደቂ ሰብ ብሓፈሻን ዝገበረልኩም ነገራት ምስ እትሓስበሉ፡ ዛጊት ብዙሕ ነገራት ከም ዝገበረ ንጹር እዩ።
1.231929
Bambo anga okha ndi amene anabwerako ndi moyo.
ኣቦይ ጥራይ ከኣ እዩ ብህይወት ተሪፉ።
1.231765
Iye anati: "Ndikupatsani inu lamulo latsopano, kuti mukondane wina ndi mnzake; monga ndakonda inu, kuti inunso mukondane wina ndi mnzake.
ኣስዕብ ኣቢሉ ኸኣ፡ "ንሓድሕድኩም ክትፋቐሩ፡ ከምቲ ኣነ ዘፍቀርኩኹም፡ ንስኻትኩም እውን ንሓድሕድኩም ክትፋቐሩ፡ ሓድሽ ትእዛዝ እህበኩም ኣለኹ።
1.231663
Iwo ali nawo maso koma iwo sakukhoza kupenya.
ኣዒንቲ ኣለዎም፡ ግናኸ ኣይርእዩን፣
1.231573
Ndimasangalala kwambiri kukhala mu utumiki tsiku lonse limodzi ndi mkazi wanga."
ምስ ሰበይተይ ምሉእ መዓልቲ ኣብ ኣገልግሎት ከሕልፎ ኸለኹ፡ ብሓቂ ዜሐጕስ እዩ" በለ።
1.23109
5 Tamverani abale anga okondedwa.
5 ፍቑራት ኣሕዋተየ ስምዑ።
1.230631
Mayi wina dzina lake Gail, yemwe panopa ali ndi zaka 60, anati: "Mwamuna wanga Robert, anamwalira pa 9 July, mu 2008, atachita ngozi.
"ብዓል ቤተይ ሮበርት ኣብ 9 ሓምለ 2008 እዩ ሞይቱ።
1.229993
Ngakhale akuchimwire maulendo 7 pa tsiku, n'kubwera kwa iwe maulendo 7, kudzanena kuti, 'Ndalapa ine,' umukhululukire ndithu."
ኣብ መዓልቲ ሸውዓተ ሳዕ እኳ እንተ በደለካ፡ 'ተጣዒሰ' እናበለ ኸኣ ሸውዓተ ሳዕ ናባኻ እንተ ተመሊሱ፡ ሕደገሉ።
1.229601
Iye ananena kuti atumwi okhulupirikawo limodzi ndi anthu ena adzalamulira ndi Yesu kumwamba.
እወ፡ እቶም እሙናት ሃዋርያትን ካልኦትን ኣብ ሰማይ ምስኡ ሓቢሮም ኪገዝኡ እዮም።
1.229484
Ndithudi Allah akudziwa, pomwe inu simudziwa (chinsinsi cha zinthu.)
እና ፈለጥኩም ዘይከውን ኣይትስርሑ።
1.229214
"Allah amafafaniza zimene wafuna ndi kulimbikitsa (kuti zisachoke zomwe wafuna), ndipo gwero la malamulo onse lili kwa Iye (Allah).
እቲ ጸጊሙ ዘሎ ሰብ ቦታ አምላኽ ሒዙ በቲ ንሱ ዝደልዮ ንኸምኡ ዝበለ ሰብ ክመርሕ ምድላዩ እዩ።
1.228941
Anthu ena ali ngati Nowa.
ገሊኦም ሰባት ከም ኖህ እዮም።
1.228871
Mawu ake anali akuti: 'Mphunzitsi wanu ndi mmodzi yekha, [Khristu] ndipo nonsenu ndinu abale.'
ይ ዝተወስደት 'ጐይታኹም ሓደ ጥራሕ እዩ ንስኹም ኩሉኹም ኣሕዋት ኢኹም' እትብል እያ።
1.228679
Kodi ndimafuna nditakhala munthu wamakhalidwe otani? - Akolose 3:10.
እንታይ ዓይነት ሰብ እየ ክኸውን ዝደሊ፧ - ቈሎሴ 3:10።
1.228636
Ngakhale babanga asadziwa pyenepi.'
ኣቦይ እውን ነዚ ይፈልጦ እዩ' በሎ።
1.228214
8 "Kudzachitika zivomezi zamphamvu."
8 'ብርቱዕ ምንቅጥቃጥ ምድሪ ኪኸውን እዩ።
1.228123
1Pe 5:6 Potero dzichepetseni pansi pa dzanja la mphamvu la Mulungu, kuti panthawi yake akakukwezeni:
6 ደጊም ብጊዜኡ ንሱ ልዕል ምእንቲ ኼብለኩም፡ ኣብ ትሕቲ እታ ጽንዕቲ ኢድ ኣምላኽ ትሕት በሉ።
1.228025
64 Koma pali ena mwa inu amene sakhulupilira.
64 ገለ ኻባኻትኩም ግና ዘይኣምኑ ኣለዉ" በሎም።
1.227925
Anthu amenewa amaona kuti safunikira Mulungu pa moyo wawo.
እዞም ሰባት እዚኦም፡ ኣምላኽ ከም ዘየድልዮም ኰይኑ እዩ ዚስምዖም።
1.227893
Kapena atamupempha nsomba, kodi angamupatse njoka?
ወይ ከዓ ዓሳ እንተለመኖ ተመን ዝህቦ?
1.227666
4 Satana sanalenge chinthu ngakhale chimodzi.
4 ሰይጣን ዋላ ሓንቲ ኣይፈጠረን።
1.227023
Pamenepo anawatseguliratu maganizo awo kuti amvetse tanthauzo la Malemba."
"ነቲ ቕዱሳት ጽሑፋት ኬስተውዕልዎ፡ ኣእምሮኦም ከፈተሎም።
1.226542
"Ndipo akadafuna Allah akadawachita iwo kukhala mpingo umodzi; koma amamulowetsa ku chifundo Chake amene wamfuna ndipo odzichitira okha chinyengo (pokana Allah) alibe mtetezi kapena mthandizi.
ኢሳይያስ ንዝደለዮ ይኽዕቦ፡ ንዝደለዮ ይኣስሮ ይቀትሎ፡ ንዝደልዮ ይሰጎ፡ ንዝደልዮ ይሸሞ።
1.226538
Sindinkadziwa chilichonse chokhudza Mulungu woona.
ብዛዕባ እቲ ናይ ሓቂ ኣምላኽ ዋላ ሓንቲ ኣይፈልጥን እየ ነይረ።
1.226481
11 Pakuti Mwana wa Munthu adadza kudzapulumutsa chotayikacho.
11 ወዲ ሰብ ንዝጠፍኤ ኼድሕን መጺኡ ኣሎ እሞ፡
1.226377
Lilime lili ndi mphamvu pa imfa ndi moyo; wolikonda adzadya zipatso zake.
ሞትን ህይወትን ኣብ ስልጣን መልሓስ እዩ፡ እቲ ዜፍቅራ ኸኣ ፍሬኣ ኺበልዕ እዩ።
1.226273
"Ndipo monga masiku a [Nowa] kotero kudzakhala kufika kwake kwa mwana wa munthu.
ከምዚ ድማ በለ፦ "ከምቲ ብዘመን ኖህ ዝዀነ፡ ወዲ ሰብ ኣብዚ ኣብ ዚህልወሉ እዋን [ወይ፡ ዳሕሮት መዓልትታት] ከኣ ከምኡ ኪኸውን እዩ።
1.225899
Ndiyeno akuti kwa ophunzira ake: "Tiyeni tipitenso ku Yudeya."
7 - ድሕርዚ ንደቀ መዛሙርቱ፡ ደጊም ንዑናይ፡ ናብ ምድሪ ይሁዳ ንኺድ፡ በሎም።
1.225323
"Ameneyu adzakhala wamkulu nadzatchedwa Mwana wa Wam'mwambamwamba.
ንሱ ዓብዪ ኪኸውን፡ ወዲ እቲ ልዑል እውን ኪብሃል እዩ፣ .
1.224535
"Sindidalenge ziwanda {Majini} ndi anthu koma kuti azindipembedza."
"ጋኔንንና (አጋንንት) ሰብን ክግዙ እለይ እምበር ንካልእ አይፈጠርኩዎምን"
1.224382
Zolakalaka za anthu oyipa sizidzachitika konse.
ת [ታው] ትምኒት እኩያት ኪጠፍእ እዩ።
1.223812
5Farao anati kwa Yosefe, "Abambo ako ndi abale ako abwera kwa iwe.
5 ፈርኦን ድማ ንዮሴፍ፤ ኣቦኻን ኣሕዋትካን መጺኦምኻ።
1.22307
Iwo anafika ponena kuti: "Ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita."
ብዝኾነ "ተግባር ኢዩ ምስክር" ኢልና ተበጊስና።
1.222839
Komabe, m'kupita kwa nthawi Solomo anakwatira akazi achilendo ambirimbiri.
ሰሎሞን ግና ካብ ካልኦት ሃገራት ብዙሓት ኣንስቲ ተመርዓወ።
1.222838
"Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.
"ንዕኡ ኸቶ እኳ እንተ ዘይረኣኹምዎ፡ ተፍቅርዎ ኢኹም።
1.222576
64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira."
Tigr 64ግና ካባኻትኩም ገሊኣቶም ዘይኣምኑ ኣለዉ፤ በሎም።
1.222463
2 Nawonso angelo ndi alaliki.
2 መላእኽቲ እውን ወንጌላውያን እዮም።
1.22208
Mwenzi utamvera malamulo anga mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje, ndi chilungamo chako monga mafunde a nyanja."
ኣየ: ትእዛዛተይ ሰሚዕካ እንተ ትኸውንሲ: ሰላምካ ኸም ወሓዚ: ጽድቅኻውን ከም ማዕበል ባሕሪ ምዀነ ነይሩ።
1.221827
Iwo anafika mpaka pokana Mwana wa Mulungu.
ሕሉፍ ሓሊፎም ንወዲ ኣምላኽ እውን ኣይተቐበልዎን!
1.221403
Limati: "Kunena za tsikulo kapena ola lake, palibe amene akudziwa, ngakhale angelo kumwamba kapenanso Mwana, koma Atate okha.
ከምዚ ዚብል ነንብብ፦ "ብዛዕባ እታ መዓልቲ እቲኣ ወይ እታ ሰዓት እቲኣ፡ ኣቦ እምበር፡ መላእኽቲ ሰማይ ኰኑ ወይስ ወዲ ዀነ፡ ሓደ እኳ ዚፈልጥ የልቦን።
1.221374
11 Mbwenye, Abheli acita cinthu cakufunika kakamwe.
11 ይኹን እምበር፡ ኣቤል ዝያዳ ኣገዳሲ ዝዀነ ነገር ገይሩ እዩ።
1.221181
Mulungu analenga anthu awiri, Adamu ndi Hava, ndipo anawauza kuti: "Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi."
ኣምላኽ ንኽልተ ሰባት፡ ማለት ንኣዳምን ንሄዋንን ፈጠሮም እሞ፡ "ፍረዩን ተባዝሑን ንምድሪ ኸኣ ምልእዋን ምለኽዋን" በሎም።
1.220932
Mudandipasa wanthu anitsogolela munjila yachadidi, nakulungama.
መገዱን ቅንዕንኡን ኣርእዩና።
1.220905
16 Mariya ankamvetsera kwambiri anthu ena akamalankhula.
16 ማርያም ብኸመይ ከም ዝሰምዐት።
1.220598
Kodi bwanji sathokoza (Allah)?
ኣግኣዚያን ይዕወትዶ ኣይዕወትን?
1.22016
Ndithudi Allah akudziwa, pomwe inu simudziwa (chinsinsi cha zinthu.)
ንዘይትፈልጦም አማልኽቲ ድማ ትሰግደሎም።
1.219655
Kodi kapolo wokhulupirika adzalandira mphoto yaikulu kumwamba kuposa odzozedwa ena?
እቲ እሙን ባርያ ኣብ ሰማይ ካብቶም ካልኦት ቅቡኣት ዝዓበየ ዓስቢ ድዩ ዚቕበል፧ ግለጽ።
1.219649
Umboni wawo ulembedwa ndipo adzafunsidwa (pazimenezo)!
ንብቕዓቶም እውን ኣብ ሕቶ የእትውዎ ይዀኑ።
1.219597
Tsiku lililonse kumabwera anzanga kudzacheza nane.
ነፍሲ ወከፍ መዓልቲ፡ ፈተውተይ ኪበጽሑኒ ይመጹ እዮም።
1.219488
Zitatero anthuwo anati: 'Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.'
ንሳቶም ከኣ፡ እግዚኣብሄር ዝበሎ ዅሉ ንገብር፡ ንእዘዝ ድማ፡ በሉ።
1.219323
Ndithudi Allah akudziwa, pomwe inu simudziwa (chinsinsi cha zinthu.)
እትፈልጦ እንተ ዘይብልካ (ዘይኰውን እኳ እንተ መሰለ) ፡ ገለ ነገር ኣይትጥቀስ።
1.219216
"Anthu anu adzadzipereka eni ake"
"ህዝብኻ ፈትዩ ይመጽእ"
1.219032
Mulungu anakupulumusa iwe pabodzi na anthu onsene."
ንሱ ኸኣ መልኣኽ ኣብ ቤቱ ደው ኢሉ፥ 'ንኢዮጴ ልኣኽ እሞ ነቲ ጴጥሮስ ዚብሃል ስምዖን ጸዊዕካ ኣምጽኣዮ፥ ንስኻን ኵሉ ቤትካን እትድኅኑሉ ቓል ንሱ ኪነግረካ እዩ፥' ኪብሎ ኸሎ ከም ዝረኣየ ነገረና።
1.218697
Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina
ስጋዊ ነገራት ዘይኰነስ፡ መንግስቲ ኣምላኽ ድለ
1.218682
10Ndimakufunafunani ndi mtima wanga wonse;
10በሙሉ ልቤ ፈለግሁህ፤
1.218605
Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse m'maso mwawo."
ኣምላኽ እውን ካብ ኣዒንቶም ንብዓት ዘበለ ኺደርዝ እዩ" ትብል።
1.218464
Choncho mdzadziwa mmene lilili chenjezo Langa (pa inu).
ማሕፉዳይ ርእዩ ፡ መዝገበይ ኣጽኒዑ
1.218343
Mulungu ndi nkulu kupiringana mitima yathu (19-24)
ኣምላኽ ካብ ልብና ይዓቢ (19-24)
1.218285
Koma akabwera, mzimu wa chowonadi, adzakutsogolelani m'choonadi chonse, pakuti sadzalankhula zake zokha, koma zomwe adzamva adzalankhula, nanena kwa inu za zinthu zomwe zikubwera. "
እቲ መንፈስ ሓቂ ምስ መጸ ግና ናብ ኩሉ ሓቂ ዘበለ ኺመርሓኩም፤ ንሱ ነቲ ዝሰምዖ ዘበለ እዩ ዚዛረብ እምበር ካብ ርእሱ ኣይዛረብን እዩ።
1.218183
Iye wakuyendayo mokwanira, nachita chilungamo, nanena zoonadi mu mtima mwake."
እቲ ብቕንዕና ዚመላለስን ጽድቂ ዚገብርን ብልቡ ሓቂ ዚዛረብን።
1.218062
Koma ngati palibe, udzabwerera kwa inu."
እንተ ዘየልቦ ግና፡ ሰላምኩም ኪምለሰኩም እዩ" በሎም።