eng
stringlengths 2
681
| nya
stringlengths 1
797
|
|---|---|
13 , 14 . ( a ) In what ways may these " critical times " cause us affliction ?
|
13 , 14 . ( a ) Kodi " nthawi zowawitsa " zingativutitse maganizo m 'njira zotani ?
|
13 USE TRANSITION TIME .
|
13 MUKAMADIKIRIRA ZINAZAKE , MUZIGWIRITSA NTCHITO NTHAWI MWANZERU .
|
15 , 16 . ( a ) Why were the Israelites warned : " Get ready to meet your God " ?
|
15 , 16 . ( a ) N 'chifukwa chiyani Aisrayeli anachenjezedwa kuti : ' Konzekera kukumana ndi Mulungu wako ' ?
|
17 , 18 . ( a ) What pattern helps us to understand the significance of ' speaking to the congregation ' ?
|
17 , 18 . ( a ) Kodi ndi chitsanzo chiti chimene chikutithandiza kumvetsa tanthauzo la ' kuuza mpingo ' ?
|
1914 Initiates a Time of Distress
|
1914 Iyambitsa Nthaŵi ya Nsautso
|
2 , 3 . ( a ) What refreshing assurance does the Bible offer in connection with acceptance ?
|
2 , 3 . ( a ) Kodi ndichiyembekezo chotonthoza mtima chotani chimene Baibulo limachipereka ponena za kulandiridwa ?
|
2 : 4 , 5 - Why does Rahab mislead the king 's men who are searching for the spies ?
|
2 : 4 , 5 - N 'chifukwa chiyani Rahabi akusocheretsa anthu a mfumu amene akusakasaka azondi aja ?
|
2 : 6 - What " gates of the rivers " were opened ?
|
2 : 6 - Kodi " zipata za mitsinje " zimene zinatsegulidwa ndi chiyani ?
|
2 Manage Your Environment
|
2 Muzichita Zinthu Zomwe Zingakuthandizeni Kukwaniritsa Zolinga Zanu
|
2 Timothy 3 : 1 - 5 signifying " the last days "
|
2 Timoteo 3 : 1 - 5 zosonyeza " masiku otsizira "
|
28 Watching the World
|
24 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
|
25 A Sea of Superlatives - But Dead !
|
25 Nyanja Yapadera Koma Yakufa
|
27 Do Not Let Illness Rob You of Joy
|
27 Musalole Kuti Matenda Akulandeni Chimwemwe
|
27 Uphold Jehovah 's Sovereignty !
|
27 Muzikhala Kumbali ya Ulamuliro wa Yehova
|
3 " We 're Letting You Go "
|
3 " Pepani , Ntchito Yanu Yatha "
|
3 , 4 . ( a ) According to one dictionary and The Watchtower , what is an organization ?
|
3 , 4 . ( a ) Malinga nkunena kwa dikishonale ina ndi Nsanja ya Olonda inayake , kodi liwu lachingelezi lotembenuzidwa kuti gulu lolinganizidwa nchiyani ?
|
3 Who Was Abraham ?
|
3 Kodi Abulahamu Anali Ndani ?
|
For Me , God Did Not Exist ( A .
|
3 Ndinkaona Kuti Kulibe Mulungu ( A .
|
4 , 5 . ( a ) What happy relationship is described at John 5 : 19 , 20 ?
|
4 , 5 . ( a ) Kodi ndiunansi wachimwemwe wotani umene ukufotokozedwa pa Yohane 5 : 19 , 20 ?
|
4 , 5 . ( a ) Through Moses , what did Jehovah set before parents as an important objective in teaching their children ?
|
4 , 5 . ( a ) Kupyolera mwa Mose , kodi Yehova anauza makolo chiyani kukhala cholinga chofunika pophunzitsa ana awo ?
|
4 The Bible 's Viewpoint
|
4 Zimene Baibulo Limanena
|
5 , 6 .
|
5 , 6 . ( a ) Kodi Eliyasibu ndi Tobia anali ndani ?
|
5 , 6 . ( a ) How widespread was fornication in the ten - tribe kingdom of Israel ?
|
5 , 6 . ( a ) Kodi chigololo chinali chofala motani mu ufumu wa Israyeli wa mafuko khumi ?
|
5 5 WORLD TRADE CENTER
|
5 5 LIKULU LA ZAMALONDA LA PADZIKO LONSE
|
4 Olympic Ideals in Crisis 8 Attaining the Ideals
|
5 Kodi Kuyang 'anitsitsa Zinthu Zosaoneka Kumavumbula Chiyani ?
|
5 What Is God 's Kingdom ?
|
5 Kodi Ufumu wa Mulungu N 'chiyani ?
|
5 What Did Jesus Teach About Hell ?
|
5 Kodi Yesu Anaphunzitsa Chiyani za Helo ?
|
Warming Reduces Infection Risk , 6 / 22
|
6 / 8
|
6 : Saved in a vessel
|
6 : Anapulumukira m 'chingalawa
|
6 / 10
|
7 / 10
|
7 : 24 - 27 Since I am responsible for directing my own life , how can I be better prepared for storms of difficulty and floods of trouble ?
|
7 : 24 - 27 Popeza ndili ndi udindo wolamulira moyo wanga , kodi ndingatani kuti ndikhale wokonzeka kulimbana ndi mavuto ndiponso masautso ambiri amene ndingakumane nawo ?
|
1 / 06
|
8 / 06
|
10 / 09
|
8 / 09
|
8 average years in the full - time ministry
|
8 Avereji ya zaka zimene akhala akuchita utumiki wa nthawi zonse
|
9 , 10 . ( a ) What dangers may some gatherings present ?
|
9 , 10 . ( a ) Kodi macheza ena angakhale ndi ngozi zotani ?
|
KANGAROOS , koalas , wombats , and platypuses , Ayers Rock and the Great Barrier Reef - these are names that come to mind when people think of Australia .
|
A KANGAROO , a koala , a wombat , ndi ma platypus , thanthwe la Ayers Rock ndi materezi a Great Barrier Reef - maina ameneŵa amabwera m 'maganizo pamene anthu aganiza za Australia .
|
We five Witnesses were sent to a prison camp in Russia .
|
A Mboni asanufe tinaikidwa mu msasa wandende wa ku Russia .
|
Jehovah 's Witnesses are known worldwide for choosing nonblood management of their medical conditions .
|
A Mboni za Yehova amadziwika pa dziko lonse kuti akadwala amafuna kulandira mankhwala opanda magazi .
|
Jehovah 's Witnesses would be happy to help you study the Bible .
|
A Mboni za Yehova angakuthandizeni kudziwa zimene Baibulo limaphunzitsa .
|
Minos Kokkinakis with his wife
|
A Minos Kokkinakis ndi akazi ŵawo
|
Robert : The verse says they 'll reside on the earth .
|
A Owen : Lembali lanena kuti adzakhala padziko lapansi .
|
" None of us involved in those early days of Aids could have imagined the scale of the epidemic that has unfolded , " says Peter Piot , executive director of the Joint United Nations Programme on HIV / AIDS ( UNAIDS ) .
|
A Peter Piot , omwe ndi mkulu wa nthambi ya bungwe la United Nations yoona za matendaŵa yotchedwa UNAIDS anati : " Pa anthu tonse amene tinkalimbana ndi matenda a Edzi atangobwera kumene panalibe aliyense amene ankaganizako zakuti matendaŵa angadzasanduke mliri waukulu motere . "
|
Marcus : Thank you .
|
A Samson : Zikomo kwambiri .
|
The Sopherim ( Jewish scribes ) changed this text long ago because they felt the original passage showed irreverence toward God .
|
A Sopherim ( alembi Achiyuda ) anasintha lembali kalelo chifukwa analingalira kuti ndime yoyambirirayo sinasonyeze ulemu kwa Mulungu .
|
The great crowd work alongside anointed Christians in preaching the good news that soon God will rock the nations at Armageddon .
|
A khamu lalikulu akugwira ntchito limodzi ndi Akristu odzozedwa polalikira uthenga wabwino wakuti posachedwapa Mulungu adzagwedeza amitundu pa Armagedo .
|
TANTRUMS
|
AKAYAMBA KUVUTA
|
WHEN in the city of Athens , the apostle Paul went every day to the marketplace to preach the good news about Jesus .
|
ALI mu mzinda wa ku Atene , mtumwi Paulo ankapita tsiku lililonse ku msika kukalalikira uthenga wabwino wa Yesu .
|
RESCUED by a miracle - what a faith - strengthening experience !
|
ANAPULUMUTSIDWA mozizwitsa - chinali chokumana nacho cholimbitsa chikhulupiriro chotani nanga !
|
THOUSANDS of couples began married life in the warm glow of love - or in the heat of passion - and expected happiness to follow .
|
ANTHU ena amalowa m 'banja atadziwana bwino pachibwenzi n 'kuyamba kukondana kwambiri . Ena amalowa m 'banja chifukwa chongotengeka mtima atakhala pachibwenzi kwa kanthawi kochepa chabe .
|
AVERAGE BIBLE STUDIES : 108,948
|
AVAREJI YA MAPHUNZIRO A BAIBULO : 108,948
|
WHEN the Jewish exiles entered ancient Babylon , they saw a city filled with idols and found a people enslaved to wicked spirits .
|
AYUDA atatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo , anapeza kuti anthu amumzindawo ankakonda kulambira mafano komanso ankachita zamizimu .
|
The Ammonites lived in this area
|
Aamoni anakhala m 'dera ili
|
In that sense , work brings an intense feeling of satisfaction .
|
Aaron , amene tamutchula m 'nkhani yoyamba ija , anati : " Ndikamaweruka kuntchito , ndimakhala nditatopa chifukwa chogwira ntchito mwakhama tsiku lonse .
|
As soon as the German brothers understood that the adjustments were in no way a criticism of their work - but that the time had come for closer cooperation between the various branches and headquarters - they were enthused and filled with a fine spirit of cooperation .
|
Abale a ku Germany atazindikira kuti kusinthaku sikuti kunali kosuliza ntchito yawo , koma kuti nthaŵi yakwana yoti nthambi zosiyanasiyana limodzi ndi likulu la padziko lonse la Mboni za Yehova zigwirire ntchito pamodzi , anayamba kunyadira kwambiri ndiponso anagwirizana nazo kwambiri .
|
I know I would never have enjoyed such loving care if I were not serving Jehovah .
|
Abale nawonso amadzipereka kunditengera kumisonkhano mlungu uliwonse .
|
Christian marriage mates who have serious problems should seek help from the elders .
|
Abale ndi alongo amene ali ndi mavuto aakulu a m 'banja ayenera kuuza akulu .
|
The brothers interviewed me and recommended that I finish my schooling , obtain a license , and then come to Bethel .
|
Abalewo anandifunsa nandiuza kuti ndimalize kuphunzira kwanga , kulandira laisensi , ndiyeno ndidzabwere ku Beteli .
|
Abraham showed that he was governed by faith not merely in isolated circumstances but throughout his life .
|
Abrahamu anasonyeza kuti anali kutsogozedwa ndi chikhulupiriro , osati pazochitika zoŵerengeka zokha , koma pa moyo wake wonse .
|
It was Abraham 's determination not to let any conflict damage their relationship .
|
Abrahamu anatsimikiza mtima kuti salola mkangano uliwonse uwononge ubale wawo .
|
Knowledge will help them to be of support , recognize important symptoms , and know how to respond .
|
Achibalewo akadziŵa bwino matendaŵa , angathandizepo mosavuta , angazindikire zimene zimachitika matendawo akam 'tengetsa munthu , ndiponso mmene angam 'thandizire zikafika potero .
|
Young people have many pressures today .
|
Achichepere ali ndi zipsinjo zambiri lerolino .
|
Many young people qualify for baptism .
|
Achichepere ambiri amayeneretsedwa kaamba ka ubatizo .
|
3 / 09 How Control Temper ?
|
Achinyamata Kodi Mungathane Bwanji ndi Mavuto Anu ?
|
Young people can gain the skills they need for adulthood .
|
Achinyamata akhoza kuphunzira luso linalake lomwe lingadzawathandize akadzakula .
|
Many youths endeavor to live up to their dedication by reaching out for the full - time ministry .
|
Achinyamata ambiri amayesetsa kukhala mogwirizana ndi kudzipatulira kwawo mwa kuchita utumiki wa nthaŵi zonse .
|
Adam and Eve chose to rebel .
|
Adamu ndi Hava anasankha kupanduka .
|
Enemies of Mankind
|
Adani a Anthu
|
He will wipe out tears of grief .
|
Adzachotsa misozi yonse ya chisoni .
|
He will deliver the poor one crying for help , also the afflicted one and whoever has no helper .
|
Adzapulumutsa waumphaŵi wofuulayo ; ndi wozunzika amene alibe mthandizi .
|
He will accept our worship , our spiritual grain offering and drink offering .
|
Adzatilola kumlambira , ndipo adzalandira nsembe yathu yaufa yauzimu ndi nsembe yothira .
|
He will abyss them along with their leader , Satan , in a state of inactivity .
|
Adzaziponya izo m 'phompho pamodzi ndi mtsogoleri wawo , Satana , mumkhalidwe wosachita kanthu .
|
The Pharisees and the scribes prided themselves on their supposed punctilious adherence to the Mosaic Law , a sort of legalistic righteousness .
|
Afarisiwo ndi alembiwo ankanyadira kumamatira kwawo ku Chilamulo cha Mose mosamalitsa , mtundu wa chilungamo chamwambo .
|
Africa - Dance of the Hooded Egunguns
|
Africa - Gule wa Egunguns
|
Put your arms around them , as Jesus did .
|
Afungatireni , monga momwe Yesu anachitira .
|
The Israelites had to pay the reasonable taxes set out by the Mosaic Law .
|
Aisrayeli anayenera kupereka msonkho woyenera malinga ndi Chilamulo cha Mose .
|
Prisoners Become Christian Ministers
|
Akaidi Akhala Atumiki Achikristu
|
As adults , they suffer the consequences of these things .
|
Akakula amadzavutika kwambiri chifukwa cha zimenezi .
|
If the tract is accepted :
|
Akalandira kapepalako :
|
Spotted leopards are nearly invisible where they lie , draped elegantly over the upper boughs of trees , camouflaged by the dappled light under the foliage .
|
Akambuku si kwapafupi kuwaona kuti agona pati , chifukwa amakhala ali phe m 'mitengo pamwamba , atabisika m 'masamba .
|
If he had died , it is likely that the kendo case would have ended without the Supreme Court decision .
|
Akanafa , kuli kwachionekere kuti mlandu wa kendo ukanatha popanda chigamulo cha Bwalo Lapamwamba .
|
If only he had considered the " end afterward " ! - Proverbs 7 : 22 , 23 .
|
Akanaganizira kaye " chitsiriziro chake " sakanayerekeza n 'komwe kuchita zimenezi . - Miyambo 7 : 22 , 23 .
|
Supervisors in this setting must learn how to deliver the " hard message so that it comes across clean , crisp and professional , and keeps the individual 's dignity intact , " reports The Vancouver Sun .
|
Akapitao amene ali mumkhalidwewu ayenera kuphunzira mmene angaperekere " uthenga wovuta kwambiri umenewu kotero kuti umveke bwino , mosavuta ndipo mwaukatswiri , ndi kusungitsa ulemu wa munthuyo , " ikutero The Vancouver Sun .
|
Then they are on their own .
|
Akatero amayamba kudziyang 'anira okha .
|
Only then will divine blessings overtake them .
|
Akatero m 'pamene madalitso a Mulungu adzawapeza .
|
Scholars speculate that these actually are the bones of Caiaphas .
|
Akatswiri a maphunziro akhulupirira kuti ameneŵa ndi mafupa a Kayafa .
|
Many scholars agree that under the Law , a criminal was executed before his body was hung on a stake .
|
Akatswiri ambiri amavomereza kuti malinga ndi Chilamulo , munthu wopalamula milandu ikuluikulu ankaphedwa kaye kenako n 'kupachika thupi lake .
|
Some experts feel that such an environment may result in children 's not developing the ability to bond well with others , thus making it easier for them to commit crimes against fellow humans , often without remorse .
|
Akatswiri ena amaona kuti moyo woterewu ukhoza kuchititsa ana kuti asamagwirizane ndi anzawo , motero akhoza kumachitira anthu ena zinthu zachiwawa ndipo nthaŵi zambiri amatero m 'maso muli gwaa .
|
Other experts agree .
|
Akatswiri ena amavomereza .
|
One study revealed that while the bathroom tended to be the cleanest place in the home , " the sites in the households that were contaminated with the most fecal bacteria were the sponge / dishcloths in the kitchen . "
|
Akatswiri ena ofufuza anapeza kuti ngakhale kuti kubafa kumakhala kosamalidwa bwino kwambiri kuposa malo ena onse panyumba , " zinthu monga zotsukira mbale komanso timataulo topukutira mbale ndi zimene zimakhala ndi tizilombo tambiri toyambitsa matenda . "
|
Egyptologists identify 31 " dynasties " of Egyptian kings and speak of the Old Kingdom ( Dynasties 3 - 6 ) , the Middle Kingdom ( Dynasties 11 , 12 ) , and the New Kingdom ( Dynasties 18 - 20 ) .
|
Akatswiri odziŵa za miyambo ya Igupto amazindikira " maufumu " 31 a mafumu a Igupto ndi kulankhula za Ufumu Wakale kukhala ( Maufumu 3 - 6 ) , Ufumu wa Pakati ( Maufumu 11 , 12 ) , ndi Ufumu Watsopano ( Maufumu 18 - 20 ) .
|
" It is estimated that three million Americans suffer from self - injury , and one in every 200 teenagers suffer from chronic self - injury , " say researchers Len Austin and Julie Kortum .
|
Akatswiri ofufuza , maina awo Len Austin ndi Julie Kortum , ananena kuti : " Achinyamata pafupifupi 3 miliyoni a ku America amadzipweteka okha , ndipo mmodzi pa achinyamata 200 aliwonse amachita zimenezi kwa zaka zambiri . "
|
Experts agree that the relationship with the child 's other parent can become a tough , divisive issue for a stepfamily .
|
Akatswiri oona za m 'banja amanena kuti banja likhoza kusokonekera ngati kholo lomwe likulera ana opeza siligwirizana ndi kholo lenileni la anawo .
|
Our wives remained behind and worked at the Finland branch office .
|
Akazi athu anatsala ndipo ankagwira ntchito pa ofesi ya nthambi ya ku Finland .
|
Christians have raised that question for centuries .
|
Akhristu akhala akudzifunsa funso limeneli kwa zaka zambirimbiri .
|
Many Christians have felt a debt of gratitude to Jehovah and have been motivated by it .
|
Akhristu ambiri amayamikira Yehova ndipo amaona kuti ayenera kumuchitira zinthu zina .
|
Some Christians who have been faithful for years have become so disheartened that they have even stopped attending congregation meetings and sharing in the field ministry .
|
Akristu ena amene akhala okhulupirika kwa zaka zambiri , alefuka ndipo aleka kupezeka pamisonkhano ya mpingo ndi kusagwiranso nawo ntchito yolalikira .
|
Christians who try to see people as God does will not judge by initial impressions .
|
Akristu omwe amayesa kuwona anthu monga mmene Mulungu amachitira sadzaweruza pa mawonekedwe oyambirira .
|
True Christians do not possess or use illegal drugs .
|
Akristu oona sasunga kapena kugwiritsa ntchito mankhwala oletsedwa .
|
Early Christians had that counsel available to guide them when many around them became excited over Roman gladiatorial contests .
|
Akristu oyambirira ankawalangiza zimenezi kuti ziwatsogolere pamene anthu ambiri m 'nthaŵi yawo ankasangalala ndi maseŵera omenyana achiroma .
|
They can neither help nor harm us , because " there is no work nor planning nor knowledge nor wisdom in the Grave . "
|
Akufa sangatithandize kapena kutivulaza chifukwa kumanda " kulibe kugwira ntchito , kuganiza zochita , kudziwa zinthu , kapena nzeru . "
|
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.