eng
stringlengths
2
681
nya
stringlengths
1
797
" On seeing the crowds , " the Bible says , " he felt pity for them , because they were skinned and thrown about like sheep without a shepherd . "
' Powona makamuwo , ' limatero Baibulo , ' anagwidwa m 'mtima ndi chisoni chifukwa cha iwo , popeza anali okambululudwa ndi omwazikana , akunga nkhosa zopanda mbusa . '
' I Couldn 't Stop Reading It '
' Sindinaleke Kuliŵerenga '
" We have learned that blood transfusions often pass along diseases , especially hepatitis , " says Sharon Vernon , director of the Center for Bloodless Medicine and Surgery at St .
' Tadziŵa kuti kuika mwazi kaŵirikaŵiri kumapatsira matenda , makamaka hepatitis , ' akutero Sharon Vernon , mkulu wa Center for Bloodless Medicine and Surgery pa chipatala cha St .
' We Are Your Fellow Workers '
' Tili Othandizana Nanu '
' That looks interesting , ' I thought .
' Zimenezi zikumveka zokondweretsa , ' ndinalingalira motero .
( 1 Corinthians 13 : 8a ) It can no more end or fail than Jehovah can .
( 1 Akorinto 13 : 8a ) Sichingathe konse kapena kulephera monga momwe Yehova samalephelera .
( 5 ) Set aside monthly the amount needed to satisfy each category .
( 5 ) Mwezi uliwonse , muzipatula ndalama zimene zikufunika kuti mulipirire zinthu za m 'gulu lililonse .
( Matthew 24 : 14 ) What good news ?
( Mateyu 24 : 14 , NW ) Mbiri yabwino yachiyani ?
( Article 1 ( 3 ) ) This option , however well meant , gave the League no sense of stability , and this , in turn , eroded the nations ' resolve to stick loyally to it .
( Mfundo 1 ( 3 ) ) Mosasamala kanthu kuti chosankha chimenechi chinali chabwino , chinapatsa Chigwirizanocho kusakhazikika , ndipo nakonso , kunalepheretsa maikowo kusunga chigamulo chawo chakumamatira ku icho mokhulupirika .
( Children under two years of age should not be given any medication without the advice of a doctor . )
( Musapatse ana osakwana zaka ziŵiri mankhwala ena aliwonse musanauzidwe ndi dokotala . )
( See the box " How Long Is a ' Day ' ? "
( Onani bokosi lakuti " Kodi Mulungu Analenga Dziko M 'masiku 6 Enieni ? "
( See opening picture . ) ( b ) God 's people have what guidance that can save their lives ? " STOP , LOOK , LISTEN . "
( Onani chithunzi pamwambapa . ) ( b ) Kodi n 'chiyani chimathandiza kwambiri anthu a Mulungu ?
( See opening pictures . )
( Onani chithunzi patsamba 21 . )
Could that still be true today ?
( The Bible Is True ) Kodi zimenezi n 'zimenenso zikuchitika masiku ano ?
( The Second Epistle General of Peter and the General Epistle of Jude , by Michael Green ) The Christian , then , must give evidence of his personal attachment to Jehovah by the way he lives his life . - 1 Timothy 2 : 2 ; 2 Peter 3 : 11 .
( The Second Epistle General of Peter and the General Epistle of Jude , lolembedwa ndi Michael Green ) Pamenepa , Mkristu ayenera kupereka umboni wa kugwirizana kwake kwaumwini kwa Yehova mwa njira imene amatsogozera moyo wake . - 1 Timoteo 2 : 2 ; 2 Petro 3 : 11 .
( Read 1 Timothy 2 : 5 ; Hebrews 8 : 10 . )
( Werengani 1 Timoteyo 2 : 5 ; Aheberi 8 : 10 . )
( Read 1 Timothy 6 : 17 - 19 . )
( Werengani 1 Timoteyo 6 : 17 - 19 . )
( Read 2 Corinthians 9 : 7 . )
( Werengani 2 Akorinto 9 : 7 . )
( Read Malachi 2 : 13 - 16 . )
( Werengani Malaki 2 : 13 - 16 . )
( Read Matthew 6 : 9 , 10 . )
( Werengani Mateyu 6 : 9 , 10 . )
( Read Proverbs 14 : 5 ; Ephesians 4 : 25 . )
( Werengani Miyambo 14 : 5 ; Aefeso 4 : 25 . )
( Read James 3 : 14 - 16 . )
( Werengani Yakobe 3 : 14 - 16 . )
( See Isaiah 48 : 17 . )
( Wonani Yesaya 48 : 17 . )
( Compare 1 Timothy 4 : 8 . )
( Yerekezerani ndi 1 Timoteo 4 : 8 . )
( Compare Romans 13 : 2 . )
( Yerekezerani ndi Aroma 13 : 2 . )
( Compare Genesis 18 : 2 , 3 , 33 ; 19 : 1 ; Exodus 3 : 2 - 4 ; Judges 6 : 11 , 12 , 20 - 22 . )
( Yerekezerani ndi Genesis 18 : 2 , 3 , 33 ; 19 : 1 ; Eksodo 3 : 2 - 4 ; Oweruza 6 : 11 , 12 , 20 - 22 . )
( Compare Jeremiah 5 : 30 , 31 ; 23 : 14 . )
( Yerekezerani ndi Yeremiya 5 : 30 , 31 ; 23 : 14 . )
( Examples : Yearbooks of Jehovah 's Witnesses , Jehovah 's Witnesses - Proclaimers of God 's Kingdom )
( Zitsanzo : Yearbooks of Jehovah 's Witnesses , Jehovah 's Witnesses - Proclaimers of God 's Kingdom )
( a ) What did the Jews learn from Jehovah 's discipline ?
( a ) Kodi Ayudawo anaphunziranji pa chilango cha Yehova ?
( a ) What does Psalm 56 tell us about David 's experience in Gath ?
( a ) Kodi Salmo 56 likutiuza chiyani za zomwe zinachitikira Davide ku Gati ?
( a ) What was the purpose of Ezekiel 's vision of the temple ?
( a ) Kodi cholinga cha masomphenya a Ezekieli a kachisi chinali chiyani ?
( a ) Why does Jehovah eventually bring hidden sins into the open ?
( a ) Kodi n 'chifukwa chiyani Yehova amavumbula machimo obisika ?
( a ) What resulted when the Jews rejected the Messiah ?
( a ) Kodi nchiyani chimene chinatulukapo pamene Ayuda anakana Mesiya ?
( a ) What outstanding event must happen before Armageddon ?
( a ) Kodi nchochitika chapadera chotani chimene chiyenera kuchitika Armagedo isanadze ?
( a ) When did the offering of incense in Israel become offensive to Jehovah ?
( a ) Kodi ndi liti pamene Yehova ananyansidwa ndi zofukiza zimene Aisrayeli ankapereka ?
( a ) What glorious treasure may we have , and why ?
( a ) Kodi ndichuma chaulemerero chotani chimene tingakhale nacho , ndipo chifukwa ninji ?
( a ) What is required for us to benefit from angelic help ?
( a ) Kodi tiyenera kutani kuti angelo azitithandiza ?
( a ) In this illustration , what is represented by the seed and the soil ?
( a ) Mufanizo la Yesu , kodi mbewu komanso nthaka zikuimira chiyani ?
( a ) Who is Michael , and how has he lived up to his name since 1914 ?
( a ) Ndani yemwe ali Mikayeli , ndipo ndimotani mmene iye wakhalira ndi moyo ku dzina lake chiyambire 1914 ?
( a ) What is the essence of Paul 's counsel at 1 Corinthians 7 : 10 , 11 ?
( a ) Ndi iti yomwe iri nsonga yaikulu ya uphungu wa Paulo pa 1 Akorinto 7 : 10 , 11 ?
( a ) How does God ' lead us in the tracks of righteousness ' ?
( a ) Ndimotani mmene Mulungu ' amatitsogozera ife m 'mabande a chilungamo ' ?
( b ) The fact that God fulfilled Ezekiel 's enactments should have what effect on us ?
( b ) Chenicheni chakuti Mulungu anakwaniritsa mafanizo ochitiridwa chitsanzo a Ezekieli chiyenera kukhala ndi chotulukapo chotani pa ife ?
( b ) What danger do Christians face ?
( b ) Kodi Akhristu ali pavuto lotani ?
( b ) How have Christians improved the lives of individuals , as indicated by a historian and the box below ?
( b ) Kodi Akristu awongolera motani miyoyo ya anthu , monga momwe kwasonyezedwa ndi katswiri wa mbiri yakale ndi bokosi liri pansili ?
( b ) What did Jehovah do with a view to implanting the fear of God in the hearts of his people ?
( b ) Kodi Yehova anachitanji ali ndi cholinga cha kukhomereza kuwopa Mulungu m 'mitima ya anthu ake ?
( b ) In what way did Jesus use his education ?
( b ) Kodi Yesu anagwiritsira ntchito maphunziro ake m 'njira yotani ?
( b ) How did one theologian describe the doctrine of the immortal soul ?
( b ) Kodi katswiri wina wa maphunziro a zaumulungu anachifotokoza motani chikhulupiriro cha mzimu wosafa ?
( b ) How successful were Jesus ' efforts ?
( b ) Kodi khama la Yesu linam 'pindulira ?
( b ) How is the extent of God 's knowledge of us indicated by the psalmist 's reference to the kidneys ?
( b ) Kodi kuya kwa chidziŵitso cha Mulungu pa ife kunasonyezedwa motani ndi wamasalmo mwakutchula impso ?
( b ) What can you do to help you keep your eyes on the prize ?
( b ) Kodi muyenera kuchita chiyani kuti muziyang 'anabe pa mphoto ?
( b ) Why did Hebrew Christians especially need Jehovah as their Helper ?
( b ) Kodi nchifukwa ninji Akristu Achihebri anafunadi Yehova monga Mthandizi wawo ?
( b ) What men in history have been called Great , and why ?
( b ) Kodi ndi anthu ati m 'mbiri amene atchedwa Aakulu , ndipo chifukwa ninji ?
( b ) What is our basic reason for obeying Jehovah 's commandments ?
( b ) Kodi ndi chiti chimene chiri chifukwa chathu chachikulu cha kumverera malamulo a Yehova ?
( b ) What long - term assignment did Jehovah give to Adam and Eve , and what would this require of both of them ?
( b ) Kodi ndi ntchito yotenga nyengo yaitali yotani imene Yehova anapatsa Adamu ndi Hava , ndipo kodi iyo ikafunikiranji kwa onse aŵiriwo ?
( b ) What happy proclamations will then be made ?
( b ) Kodi ndi zilengezo zosangalatsa zotani zimene zidzaperekedwa panthaŵiyo ?
( b ) What will be considered in the following article ?
( b ) Kodi tidzakambirana chiyani m 'nkhani yotsatira ?
( b ) What questions will be discussed in the following article ?
( b ) Kodi tikambirana mafunso otani m 'nkhani yotsatira ?
( b ) How can a moral collapse be avoided ?
( b ) Kodi tingapewe bwanji kuchita zinthu zolakwika ?
( b ) In what practical ways can you train new publishers and young ones to show love for their brothers and sisters ?
( b ) Kodi tingaphunzitse bwanji atsopano ndi ana kuti azikonda abale ndi alongo awo ?
( b ) With regard to Christian meetings , how may we view the use of alcoholic beverages ?
( b ) Kodi tiyenera kukhala ndi maganizo otani pa nkhani yomwa mowa tisanapite ku misonkhano ?
( b ) What are some examples of undefiled worship ?
( b ) Kodi zitsanzo zina za kulambira kosadetsedwa nziti ?
( b ) Our giving a positive response to the command " Fear God and give him glory " will result in what ?
( b ) Kupereka kwathu yankho lotsimikizirika ku lamulo la " Kuwopa Mulungu ndi kumpatsa ulemerero " kudzatulukapo chiyani ?
( b ) For dedicated servants of Jehovah and their children , what purpose should education serve ?
( b ) Kwa atumiki odzipatulira a Yehova ndi ana awo , kodi maphunziro ayenera kukhala ndi cholinga chotani ?
( b ) In 1919 what future did the former captor of Jehovah 's anointed servants have ?
( b ) M 'chaka cha 1919 kodi omwe anagwira atumiki odzozedwa a Yehova ukapolo anali ndi tsogolo lotani ?
( b ) Why may we be assured that approach to God is possible ?
( b ) N 'chifukwa chiyani tingatsimikize kuti n 'zotheka kuyandikira kwa Mulungu ?
( b ) Why must we not be devious or deceptive ?
( b ) N 'chifukwa chiyani tiyenera kupewa chinyengo ?
( b ) What is necessary for spiritual Israel to be able to rule with Christ in heaven ?
( b ) N 'chiyani chinafunika kuti Aisiraeli auzimu akalamulire ndi Khristu kumwamba ?
( b ) What are alternative readings for " might " at Isaiah 12 : 2 , and why are they also appropriate ?
( b ) Ndi kaŵerengedwe kosiyana kotani ka " nyonga " pa Yesaya 12 : 2 , NW ndipo nchifukwa ninji iko kalinso koyenera ?
( b ) How are wrongdoers " on slippery ground " ?
( b ) Ndi motani mmene ochita zoipa alili " poterera " ?
( b ) What privileges await Jehovah 's faithful servants ?
( b ) Ndi mwaŵi wotani umene ukuyembekeza atumiki okhulupirika a Yehova ?
( b ) What will then occur , and what prospect will open up before all true worshipers ?
( b ) Ndiyeno kodi nchiyani chimene chidzachitika , ndipo kodi nchiyembekezo chotani chimene chidzatseguka kwa olambira owona ?
( c ) To what did Jesus liken his preaching work , and what did he tell his disciples to do ?
( c ) Kodi Yesu anayerekeza ntchito yake yolalikira ndi chiyani , ndipo nchiyani chimene iye anauza ophunzira ake kuchita ?
( c ) In fulfillment of Genesis 3 : 15 , how was the woman 's Seed bruised in the heel ?
( c ) Pakukwaniritsidwa kwa Genesis 3 : 15 , kodi Mbewu ya mkazi anainzunzunda motani kuchitende ?
This report also said : " Religion and spirituality appear to be an important part of many children 's lives and are vital to family relationships . "
* ( Social Science Research ) Nkhani imeneyi inanenanso kuti : " Zikuoneka kuti chipembedzo komanso moyo wauzimu zathandiza ana ambiri ndipo zathandizanso kuti anthu azigwirizana m 'banja . "
* - Exodus 34 : 6 , 7 ; James 5 : 16 .
* - Eksodo 34 : 6 , 7 ; Yakobo 5 : 16 .
* He also noted that I had high blood pressure . "
* Anapezanso kuti magazi anga ankathamanga kwambiri . "
* Not all deny Jesus ' faith , however .
* Komabe , si onse amene amakana chikhulupiriro cha Yesu .
* But why does the name of God , which is the very epitome of purity and holiness , need to be sanctified ?
* Komano kodi n 'chifukwa chiyani dzina la Mulungu , lomwe ndi chizindikiro chenicheni cha udongo ndi chiyero , lifunika kuyeretsedwa ?
* In a spiritual sense , false religion has poisoned the nations , misleading them into believing in false gods and teachings that have diverted their attention from Jehovah and the issue of universal sovereignty .
* M 'lingaliro lauzimu , chipembedzo chonyenga chathira mankhwala amitundu , kuwasokeretsa iwo m 'kukhulupirira mwa milungu yonyenga ndi ziphunzitso zomwe zapatutsa chisamaliro chawo kuchoka kwa Yehova ndi nkhani ya ulamuliro wa chilengedwe cha ponseponse .
* As soon as Marilyn left , she began to suffer the gnawing pain of separation from her family .
* Marilyn amene tamutchula uja atangopita kunja , anayamba kulisowa banja lake koopsa .
* Then in 1996 we were given a similar assignment in the Fiji branch , where we were able to give support to the translation work being done in the Fijian , Kiribati , Nauruan , Rotuman , and Tuvaluan languages .
* Mu 1996 , tinapemphedwa kukatumikira kunthambi ya ku Fiji . Kumenekonso tinathandiza pa ntchito yomasulira mabuku m 'chilankhulo cha Chifiji , Chikiribati , Chinauru , Chirotuma ndi Chituvalu .
* For good reason , the Bible says : " Flee from fornication . " - 1 Corinthians 6 : 18 .
* N 'chifukwa chake Baibulo limati : " Thaŵani dama . " - 1 Akorinto 6 : 18 .
* How remarkable that this psalmist of ancient times managed to write words that harmonize so well with modern - day discoveries !
* N 'zochititsa chidwi kuti wamasalimo ameneyu analemba zinthu zimenezi kale kwambiri koma zikugwirizana ndi zimene asayansi masiku ano angotulukira kumene .
* This can be your first step in drawing closer to the " Hearer of prayer . " - Psalm 65 : 2 .
* Ndipo kuchita zimenezi kungakuthandizeni kuti mukhale bwenzi la Mulungu amene ndi " Wakumva pemphero . " - Salimo 65 : 2 .
* Hopefully , you want something better for yourself .
* Ndithudi , inu mukufuna kanthu kena kabwinopo kaamba ka inu mwini .
* Continue to take in accurate knowledge from the Bible .
* Pitirizani kuphunzira choonadi chimene chimapezeka m 'Baibulo .
* You might try talking to your parents about it in a calm , nonaccusing way .
* Yesani kulankhula nawo za nkhaniyo mofatsa , mosaŵaimba mlandu .
* This is not a morbid dread of bad consequences but , rather , a healthy , reverential regard for God and his ways .
* Zimenezi sizikutanthauza kuti tiziopa Mulungu chifukwa cha zoipa zimene zingatichitikire chifukwa chosamumvera , koma tiziopa Mulungu chifukwa choti timamulemekeza .
* That did not present a problem , as it was common for people there to speak both languages .
* Zimenezi sizinabweretse vuto lililonse chifukwa anthu ambiri mumzindawu ankalankhula zinenero zonsezi .
1 , 2 . ( a ) What trials do some of our brothers and sisters face ?
1 , 2 . ( a ) Kodi abale ndi alongo athu ena akumana ndi mavuto otani ?
1 , 2 . ( a ) What does " paradise " mean , and like what must the garden of Eden have been ?
1 , 2 . ( a ) Kodi nchiyani chomwe " paradaiso " imatanthauza , ndipo munda wa Edene uyenera kukhala unafanana ndi chiyani ?
1 , 2 . ( a ) To whom did Jesus ' words at Matthew 24 : 12 initially apply ?
1 , 2 . ( a ) Kodi ndi ndani amene analola kuti chikondi chawo chizirale m 'nthawi ya atumwi ?
10 , 11 . ( a ) How did Paul show that we should be respectful to men in authority ?
10 , 11 . ( a ) Kodi ndimotani mmene Paulo anasonyezera kuti tiyenera kukhala aulemu kwa anthu amene ali ndi ulamuliro ?
vs 10 - How was Edom " cut off to time indefinite " ?
10 - Kodi Edomu ' anawonongedwa ku nthawi yonse ' m 'njira yotani ?
10 : 34 - 38 - Is the Scriptural message to be blamed for family rifts ?
10 : 34 - 38 - Kodi uthenga wa m 'Malemba ndiwo umachititsa kuti mabanja azigawanika ?
11 , 12 . ( a ) Why does Jehovah desire Christianity to be made known ?
11 , 12 . ( a ) Kodi nchifukwa ninji Yehova akufuna kuti Chikristu chidziŵike ?
I Gave Up Lucrative Career ( M .
11 / 10
11 : 29 ; Rev .
11 : 29 ; Chiv .
11 What Kind of Star Led the " Wise Men " to Jesus ?
11 Kodi Nyenyezi Imene Inatsogolera " Anzeru a Kum 'mawa " Inali Yotani ?
12 , 13 . ( a ) What does " the public declaration of our hope " mentioned at Hebrews 10 : 23 include ?
12 , 13 . ( a ) Nchiyani chimene " kuvomereza [ poyera , NW ] chiyembekezo chathu " kotchulidwa pa Ahebri 10 : 23 kumaphatikiza ?