eng
stringlengths
2
681
nya
stringlengths
1
797
' Here is your God , Israel , ' they cried ' who brought you out of the land of Egypt ! '
' Pano pali Mulungu wako , Israyeli , ' iwo anafuula ' yemwe anakutulutsa iwe kutuluka m 'dziko la Igupto ! '
The inexperienced ones will certainly take possession of foolishness , but the shrewd ones will bear knowledge as a headdress .
Achibwana amalandira cholowa cha utsiru ; koma ochenjera amavala nzeru ngati korona .
Love never fails .
Chikondi sichitha nthaŵi zonse .
Justice - Justice You Should Pursue
Chilungamo - Chilungamo Ndicho Mudzichitsata
Remember Me , O My God , for Good
Inu Mulungu Wanga , Mundikumbukire pa Zabwino Zimene Ndinachita
He Will Rise
Iye Adzauka
TAKE a deep breath !
KHAZIKITSANI mtima pansi !
Be Peaceable With All Men
Khalani mwa Mtendere ndi Anthu Onse
To have children , to be happy and then to die .
Kukhala ndi ana , kukhala wachimwemwe ndiyeno kufa .
The plenty belonging to the rich one is not permitting him to sleep .
Kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo .
Make my joy full in that you are . . . doing nothing out of contentiousness or out of egotism , but with lowliness of mind considering that the others are superior to you , keeping an eye , not in personal interest upon just your own matters , but also in personal interest upon those of the others .
Kwaniritsani chimwemwe changa , . . musachite kanthu monga mwa chotetana , kapena monga mwa ulemerero wopanda pake , komatu ndi kudzichepetsa mtima , yense ayese anzake omposa iye mwini ; munthu yense asapenyerere zake za iye yekha , koma yense apenyererenso za mnzake .
YOU HAVE ACTED FOOLISHLY
MWACHITA ZOPUSA
Jehovah 's Witnesses Protected Me !
Mboni za Yehova Zandichinjiriza !
God Is Greater Than Our Hearts
Mulungu Ali Wamkulu Woposa Mitima Yathu
With oil you have greased my head .
Mwandidzoza mutu wanga mafuta .
I FEEL scared and excited at the same time !
NDIMAKHALA wamantha ndi wachimwemwe panthaŵi imodzimodzi !
I went flying off the tracks and fell down on the cinders just beyond .
Ndinanyamuka panjanjipo ndi kugwera m 'mapulusa a malasha amene anali m 'mbali mwake .
' Tribulation in the Flesh '
Nsautso M 'thupi
The works of his hands are truth and judgment ; trustworthy are all the orders he gives , well supported forever , to time indefinite , done in truth and uprightness .
Ntchito za manja ake ndizo choonadi ndi chiweruzo ; malangizo ake onse ndiwo okhulupirika . Achirikizika ku nthawi za nthawi , achitika m 'choonadi ndi chilunjiko .
We Are Missing Some Fundamental Element
Pali Mbali Ina Yofunika Imene Ikusoŵeka
Why pay when you can get it free ?
Palibe chifukwa choperekera ndalama pa zinthu zomwe munthu ukhoza kuzipeza mwaulere .
By the 1980s belief in the Devil had disappeared except among conservative Catholics , charismatics , conservative Protestants , Eastern Orthodox , Muslims - and a few occultists .
Pofika mu ma 1980 chikhulupiriro mwa Mdyerekezi chinazimiririka kuchotsapo kokha pakati pa Akatolika enieni , magulu opatuka kuchoka ku chiProtestanti , Aprotestanti enieni , Eastern Orthodox , Asilamu - ndi okhulupirira malaulo ochepa .
I Have Not Sat With Men of Untruth
Sindinakhala Pansi ndi Anthu Achabe
I 've Never Seen Anything Like This !
Sindinaonepo Zonga Zimenezi !
We mustn 't let our spirit lose its sparkle
Tisalole kuti changu chathu chizirale n 'kusiya kunyezimira
Jehovah , Please Let Me Serve You
Yehova , Ndiloleni Kuti Ndikutumikireni
It is too much to bear .
Zimakhala zovuta zedi kuzipirira .
" 2000 is , in a way , ' the largest expected event ' in human history ever , " suggests social researcher Bernward Joerges of Berlin , Germany .
" 2000 , m 'njira inayake , iri ' chochitika chachikulu choyembekezeredwa ' chikhalire m 'mbiri ya anthu , " akulingalira tero Bernward Joerges wofufuza zamayanjano a anthu wa ku Berlin , Jeremani .
" When these delegates first arrived , they were very nervous and timid , " relates a Christian who helped with rooming .
" Alendo ameneŵa atangofika kumene , anali ndi nkhaŵa komanso manyazi kwambiri , " anatero Mkristu wina amene anali kuthandiza nawo pantchito yokonzera alendowo malo ogona .
" My mother never sits down and has a talk with me , " complained one young girl .
" Amayi samakhala konse pansi kukambirana nane nkhani , " anadandaula msungwana wina wachichepere .
" No , " she called back , a little bewildered .
" Ayi , " iye anatero , ali wododoma pang 'ono .
" Faith is the assured expectation of things hoped for . " - HEBREWS 11 : 1 .
" Chikhulupiriro ndicho chikhazikitso cha zinthu zoyembekezeka , chiyesero cha zinthu zosapenyeka . " - AHEBRI 11 : 1 .
Acts of " affection " can become increasingly inappropriate or unclean .
" Chikondi " chotere chingakule n 'kufika posafunikira kapenanso ponyansa .
" The sad situation is that . . . the pharmaceutical industry isn 't looking for [ new treatments ] , " says Michael Ferguson , a molecular biologist at the University of Dundee , Scotland .
" Chomvetsa chisoni n 'chakuti . . . makampani opanga mankhwala sakufufuzanso mankhwala [ atsopano ] , " anatero Michael Ferguson yemwe ndi katswiri wa sayansi pa yunivesite ya Dundee ku Scotland .
" Men in Western civilization have thus been thrown back wholly on themselves , and they find themselves wanting , " concludes The Columbia History of the World .
" Chotero , anthu m 'kutsungula Kwakumadzulo akhala akudalira kotheratu pa iwo okha , ndipo amadzipeza kukhala opereŵera , " ikumaliza motero The Columbia History of the World .
" Granny " Hamilton became the first baptized publisher in County Longford . - 1 Thessalonians 2 : 13 .
" Gogo " Hamilton anakhala wofalitsa wobatizidwa woyamba mu County Longford . - 1 Atesalonika 2 : 13 .
" He will swallow up death forever , and the Sovereign Lord Jehovah will wipe away the tears from all faces . " - Isaiah 25 : 8 .
" Iye adzameza imfa kwamuyaya ndipo Yehova , Ambuye Wamkulu Koposa , adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu . " - Yesaya 25 : 8 .
" Trust in Jehovah , you people , for all times , for in Jah Jehovah is the Rock of times indefinite . " - ISAIAH 26 : 4 .
" Khulupirirani Yehova anthu inu , nthaŵi zamuyaya , pakuti mwa Ya Yehova muli Thanthwe lachikhalire . " - YESAYA 26 : 4 , NW .
[ God 's ] undeserved kindness that was toward me did not prove to be in vain , but I labored in excess of [ all the other apostles ] . " - 1 Corinthians 15 : 9 , 10 .
" Koma . . . chisomo [ cha Mulungu ] cha kwa ine sichinakhala chopanda pake , koma ndinagwirira ntchito yochuluka ya [ atumwi ena onse ] . " - 1 Akorinto 15 : 9 , 10 .
" Be transformed by making your mind over , that you may prove to yourselves the good and acceptable and perfect will of God , " says the apostle Paul .
" Koma mukhale osandulika , mwa kukonzanso kwa mtima wanu , kuti mukazindikire chimene chili chifuno cha Mulungu , chabwino , ndi chokondweretsa , ndi changwiro , " akutero mtumwi Paulo .
Liquid Gold ( olive oil ) , 4 / 08
" Kukonda Kwambiri Anthu " ( Russia ) , 8 / 08
" Making new friends was really the key [ to adjusting ] , " says a youth named Brian whose family moved to the southern part of the United States .
" Kupanga mabwenzi atsopano kunalidi mfungulo [ ya kusintha ] , " akutero wachichepere wina wotchedwa Brian amene banja lake linasamukira kumbali yakummwera kwa United States .
" The prevention of violence in the home and the reduction of family violence involve major structural changes for both the society and the family . " - Behind Closed Doors .
" Kupewa ndewu muukwati ndi kuchepetsa ndewu m 'banja kumaphatikizapo masinthidwe aakulu amachitidwe kwa onse aŵiri chitaganya ndi banja . " - Behind Closed Doors .
" Career decision making is one of the major challenges young people face , " says the book Career Coaching Your Kids .
" Kusankha zinthu zoti mudzachite mutakula , n 'chinthu chovuta kwambiri kwa achinyamata , " linatero buku lakuti Career Coaching Your Kids .
" In the fourth year of Jehoiakim the son of Josiah , the king of Judah , " the word of the Great Timekeeper " occurred to Jeremiah concerning all the people of Judah . "
" M 'chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu mwana wa Yosiya , mfumu ya Yuda , " Yehova anauza Yeremiya mawu okhudza anthu a ku Yuda .
" THE reasonable man " - English journalist Sir Alan Patrick Herbert dubbed him a mythical figure .
" MUNTHU wololera " - Mtolankhani Wachingelezi Bwana Alan Patrick Herbert anamutcha kukhala munthu wa m 'nthano chabe .
" The calamitous days " of old age may hinder elderly Christians from serving Jehovah with the vigor they once had . - Ecclesiastes 12 : 1 .
" Masiku oipa " a ukalamba angalepheretse Akristu okalamba kutumikira Yehova ndi mphamvu monga kale . - Mlaliki 12 : 1 .
This " reproductive seed " is God 's holy spirit .
" Mbewu " imeneyi ndiyo mzimu woyera wa Mulungu .
" My Sister Never Gave Up on Me . " - YELENA VLADIMIROVNA SYOMINA
" Mchemwali wanga sanataye mtima . " - YELENA VLADIMIROVNA SYOMINA
" A wife should not depart from her husband ; . . . and a husband should not leave his wife . " - 1 CORINTHIANS 7 : 10 , 11 .
" Mkazi asasiye mwamuna wake ; . . . mwamuna asalekane naye mkazi . " - 1 AKORINTO 7 : 10 , 11 .
" Unlike many of my former friends who are now dead , I am alive and enjoying a happy family life , " says Adrian .
" Mosiyana ndi ambiri mwa azinzanga omwe tsopano anamwalira , ine ndili moyo ndipo ndili ndi banja lachimwemwe , " anatero Adrian .
" This means everlasting life , " Jesus said in prayer , " their taking in knowledge of you , the only true God , and of the one whom you sent forth , Jesus Christ . " - John 17 : 3 .
" Moyo wosatha ndi uwu , " anatero Yesu m 'pemphero , " kuti akadziŵe Inu Mulungu woona yekha , ndi Yesu Kristu amene munam 'tuma . " - Yohane 17 : 3 .
" Life , " he reminded me , " is far better traversed with as little baggage as possible .
" Moyotu , " iwo anandikumbutsa motero , " umakhala bwinopo ndi zinthu zochepa zakuthupi .
" The birdcatcher , " Satan , sets many traps .
" Msodzi , " Satana , amatchera misampha yambirimbiri .
" Choose for yourselves today whom you will serve , " he said .
" Mudzisankhire lero amene mudzamtumikira , " anatero .
" That 's very impressive , Tiffany , that is very impressive , " said the teacher over and over again .
" N 'zochititsa chidwi kwambiri zimenezi , Tiffany , n 'zochititsa chidwi kwabasi , " anatero mphunzitsiyo mobwerezabwereza .
" It is a privilege to receive an assignment from Jehovah God through his organization , " stated Mark Noumair , who served as a missionary in Kenya for 11 years and is now a Gilead instructor .
" Ndi mwaŵi kulandira gawo la ntchito kuchokera kwa Yehova Mulungu kudzera m 'gulu lake , " anatero Mark Noumair , amene anatumikira monga mmishonale ku Kenya kwa zaka 11 ndipo tsopano ndi mlangizi wa ku Gileadi .
" They are the only ones to go from door to door with ' the good news , ' applying the Bible 's principles . " - Życie Literackie , Poland .
" Ndi okhawo omwe amapita khomo ndi khomo ndi ' uthenga wabwino , ' kugwiritsa ntchito mfundo zachikhalidwe chabwino za m 'Baibulo . " - Nyuzipepala ya Życie Literackie , ku Poland .
" I jump for joy now , " he says , " when I think of what Jehovah God and Jesus Christ have done and will yet do for us ! "
" Ndimadumpha ndi chisangalalo tsopano , " iye akutero , " pamene ndiganiza za zimene Yehova Mulungu ndi Yesu Kristu atichitira ndipo adzatichitirabe ! "
" My life is dedicated to the service of the Most High , " read the press report , " and I cannot serve two masters . "
" Ndinapatulira moyo wanga kuchita utumiki wa Wam 'mwambamwamba , " inasimba motero nyuzipepala , " ndipo sindingatumikire ambuye aŵiri . "
" I prayed with my eyes open , " she recalls .
" Ndinapemphera osatseka maso , " iye anatero pokumbukira .
" I learned responsibility , " says a young man named Eric .
" Ndinaphunzira kukhala wathayo , " akutero mnyamata wachichepere wotchedwa Eric .
" I began this whole diet to control my weight , but now it 's controlling me , " says Jaimee .
" Ndinayamba khalidwe losala kudya limeneli chifukwa choti ndimafuna kuonda koma m 'malo mwake khalidweli likundilamulira , " akutero Jaimee .
" You 're still a woman , and I 'm still a man . " )
" Ndiwe mkazi ndithu , inenso ndine mwamuna ndithu . " )
" It is easy to let yourself go , to collapse and be consumed in self - pity " when exposed to a hostile or dangerous environment , says The SAS Survival Handbook .
" Nkwapafupi kugonja , kulephera ndi kungodzichitira chisoni " mutakhala pamalo oipa kapena angozi , ikutero The SAS Survival Handbook .
At times I say things that everyone is probably thinking but that shouldn 't be said out loud . . .
" Nthawi zina ndimanena zinthu zomwe anthu enanso akuganiza koma zoti n 'zosayenera kunena pagulu . " - Allie
You Can Remain Morally Clean , 11 / 1
" Nthaŵi Yake Siinafike , " 9 / 15
" Sometimes we have pizza night , " says Sanchia , a girl from South Africa .
" Nthaŵi zina timadya pizza usiku , " akutero Sanchia , msungwana wa ku South Africa .
" Studies show that the divorce rate in shift working families is 60 percent higher than for day workers in regular jobs , " says the book The 24 - Hour Society .
" Ofufuza amasonyeza kuti chiŵerengero cha kusudzulana m 'mabanja ogwira ntchito za mashifiti ndi chokwera ndi maperesenti 60 kuposa cha ogwira ntchito masana , " limatero buku lakuti The 24 - Hour Society .
" With you [ God ] is the source of life . " - Psalm 36 : 9 .
" Pakuti inu [ Mulungu ] ndinu kasupe wa moyo . " - Salimo 36 : 9 .
" When I 'm really in trouble or just do some stupid thing around the house , " laments 16 - year - old Karl , " they 'll say , ' Alan doesn 't do that ' or , ' Why can 't you clean up your room like Alan ? ' "
" Pamene ndiridi m 'vuto kapena ndachita kanthu kena kopusa panyumba , " anadandaula motero Karl wazaka 16 zakubadwa , " iwo adzati , ' Alan samachita zimenezo ' kapena kuti , ' Kodi ulekeranji kuyeretsa chipinda chako ngati Alan ? ' "
" Although he was existing in God 's form , " Jesus " gave no consideration to a seizure , namely , that he should be equal to God . "
" Pokhala nawo maonekedwe a Mulungu , " Yesu " sanachiyesa cholanda kukhala wofanana ndi Mulungu . "
" Concerning that day or the hour , " Jesus said , " nobody knows , neither the angels in heaven nor the Son , but the Father . " - Mark 13 : 32 , 33 .
" Ponena za tsikulo ndi ora , " Yesu anati , " palibe aliyense adziŵa , ngakhale angelo m 'mwamba kapena Mwana , koma Atate ndiwo . " - Marko 13 : 32 , 33 .
" Find exquisite delight in Jehovah , and he will grant you the desires of your heart . " - PS .
" Sangalala mwa Yehova , ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako . " - SAL .
" Ornament of All Galilee " ( Sepphoris ) , 6 / 1
" Sankhani Moyo Kuti Mukhale ndi Moyo , " 6 / 1
" I shall not speak much with you anymore , " he says , " for the ruler of the world is coming . And he has no hold on me . "
" Sindidzalankhulanso zambiri ndi inu , " iye akutero , ' pakuti mkulu wa dziko lapansi adza ; ndipo alibe kanthu mwa Ine . '
" I no longer call you slaves , " he told them , " because a slave does not know what his master does . But I have called you friends , because all the things I have heard from my Father I have made known to you . "
" Sinditchanso inu akapolo , " anawauza tero , " chifukwa kapolo sadziŵa chimene mbuye wake achita ; koma ndatcha inu abwenzi ; chifukwa zonse zimene ndazimva kwa Atate wanga ndakudziŵitsani . "
" We would not have been able to convince people in America , Canada or Japan to stop buying ivory if we were still selling it , " he replied .
" Sitikanatha kukhutiritsa maganizo mwamphamvu anthu a ku Amereka , Canada kapena Japan kuti aleke kugula minyanga ya njovu ngati tikanapitiriza kuigulitsa , " iye anayankha motero .
" We are filled with gratefulness and appreciation for being Jehovah 's guests here in Berlin amid an international brotherhood . " - Bernd .
" Tadzazidwa ndi chikondwerereo ndi chiyamikiro cha kukhala alendo a Yehova muno mu Berlin pakati paubale wa m 'mitundu yonse . " - Bernd .
" The church has been lying to us , " I said .
" Tchalitchi chakhala chikutinamiza , " ndinatero .
" We have this treasure in earthen vessels , that the power beyond what is normal may be God 's and not that out of ourselves . " - 2 Corinthians 4 : 7 .
" Tili nacho chuma ichi m 'zotengera zadothi , kuti ukulu woposa wamphamvu ukhale wa Mulungu , wosachokera kwa ife . " - 2 AKORINTO 4 : 7 .
" We became gentle in the midst of you , as when a nursing mother cherishes her own children . " - 1 THESSALONIANS 2 : 7 .
" Tinakhala ofatsa pakati pa inu , monga mmene mlezi afukatira ana ake a iye yekha . " - 1 ATESALONIKA 2 : 7 .
" It should not be overlooked that one of [ Lucaris ' ] primary aims was to enlighten and uplift the educational level of his clergy and flock , which in the sixteenth and early seventeenth century had sunk to an extremely low point , " states one scholar .
" Tisaiwale mfundo yakuti chimodzi mwa zolinga zikuluzikulu za [ Lucaris ] chinali kuzindikiritsa ndi kukweza maphunziro a atsogoleri ake a chipembedzo ndi nkhosa , omwe m 'zaka za zana la 16 ndi kumayambiriro kwa zaka za zana la 17 anali ataloŵeratu pansi , " akutero katswiri wina wa zamaphunziro .
" The day of Jehovah " was imminent , and his face was set against those ' withdrawing from him , ' that is , ' dedicating themselves away from following God . '
" Tsiku la Yehova " linayandikira , ndipo nkhope yake inalunjikitsidwa motsutsana ndi awo ' ochoka kwa iye , ' kunena kuti , ' odzipereka iwo eni kuchoka ku kutsatira Mulungu . '
" Poverty in juxtaposition to great wealth " is one that was referred to by the Nigerian inspector - general of police .
" Umphaŵi woyendera limodzi ndi kulemera kwambiri " ndiwo chimodzi cha zinthuzo chimene mkulu wa apolisi wa ku Nigeria anatchula .
" The vaccinator has replaced the postman as the most familiar visitor to home and hamlet , " notes a report on EPI .
" Wakatemera amachezera kwambiri nyumba ndi midzi kuposa wamtokoma , " lipoti lonena za EPI likutero .
Those " meals " were delicious - and they nourished us well spiritually .
" Zakudya " zimenezo zinali zokoma ndipo zinatipatsa thanzi labwino lauzimu .
" All things , therefore , that you want men to do to you , you also must likewise do to them . " - Matthew 7 : 12 .
" Zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni , inunso muwachitire zimenezo . " - Mateyo 7 : 12 .
' He feared God and turned aside from bad . '
' Anaopa Mulungu ndi kupewa zoipa . '
' It is by your life course once you get there , ' he stressed .
' Chiri mwa njira yanu ya moyo mwamsanga mutafika kumeneko , ' iye anagogomezera .
' The Truth That Sets Us Free '
' Choonadi Chomwe Chimatimasula '
They That Go Down to the Sea in Ships
' Iwo Akutsikira Kunyanja M 'zombo '
Be Content
' Khalani Okhutira '
' Keeping my regulations , ' he said , " is wisdom on your part and understanding on your part before the eyes of the peoples who will hear of all these regulations , and they will certainly say , ' This great nation is undoubtedly a wise and understanding people . ' " - Deuteronomy 4 : 5 - 7 .
' Kusunga maweruzo anga , ' iye anatero , " ndi nzeru zanu ndi chidziŵitso chanu pamaso pa mitundu ya anthu akumva malemba ndi kuti , Ndithu mtundu waukulu uwu , ndiwo anthu anzeru ndi akuzindikira . " - Deuteronomo 4 : 5 - 7 .
' His Mouth Is a Source of Life '
' M 'kamwa Mwake Ndi Kasupe wa Moyo '
12 / 1 ' At River Coco , Turn Right , ' 9 / 1
' Mulungu Ndi Amene Amakulitsa ' !
I Will ' Climb Up Just as a Stag Does ' ( August 2006 ) Francesco Abbatemarco 's patience and humility really made me think .
' Ndidzadumpha Ngati Nswala ' ( August 2006 ) Kupirira ndi kudzichepetsa kwa Francesco Abbatemarco , kunandichititsa kuganiza mozama .
Do Not ' Follow the Crowd '
' Osatsata Unyinji wa Anthu '
It is God 's minister to you for your good .
' Pakuti ndiye mtumiki wa Mulungu , kuchitira iwo zabwino .
' Continue to Be Readjusted '
' Pitirizani Kukhala Wowongolereka '