score
float32
1.04
1.25
Bemba
stringlengths
9
497
Chichewa
stringlengths
9
500
1.249897
Kakuli coko ya ka i bubebe, mi mulwalo wa ka ha u na bukiti."
Pakuti goli langa ndi losavuta ndipo katundu wanga ndi wopepuka."
1.249783
Natani alilabiile ati: "Kamucita fyonse ifili mu mutima wenu; pakuti baLesa bali nenu."
Natani anati: "Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu, chifukwa Mulungu woona ali nanu."
1.249781
Kabili Sekaria pakumona alisakamikwe, no mwenso walimwikete.
Ndipo Zekariya anadabwa pamene anamuona, ndipo mantha anamgwira.
1.249731
Lelo nshilemona ifyo fileampana na 1914.
Komabe sindikuona kugwirizana kwa zimenezi ndi chaka cha 1914.
1.249613
Bushe ali no kuupa umwanakashi na umbi?
Kodi iye adzakwatira mkazi wina?
1.249576
"Tata untabukile bukata" (28)
"Baba ndi nkulu kupiringana ine" (28)
1.249538
Cisuma ukukwata abanobe abengi."
Zimakhala bwino kukhala ndi anzako ambiri."
1.249382
5Pantu Lesa alishiba ukuti ilyo mukalyako, amenso yenu yakesuka elyo mukaba nga Lesa, mukeshiba ifisuma ne fibi."
5Pakuti Mulungu akudziwa kuti tsiku lomwelo la YANU kudya zipatso zake YANU maso adzatseguka ndipo inu adzakhala ngati Mulungu, WODZIWA zabwino ndi zoipa. "
1.249108
Myaka 12 pa kupita'po, twetana nandi monka mu New York.
Patapita zaka 12, tinakumananso ku New York.
1.249058
Ifipande fyaba muli Loleni! ifitila "Abacaice Bepusha Ukuti"
Nkhani za mu Galamukani! zakuti, "Zimene Achinyamata Amadzifunsa"
1.248978
October 2015 _ Amepusho Yatatu ayo Abantu Bengatemwa Ukwipusha Lesa
October 2015 _ Mafunso Atatu Omwe Anthu Amafuna Atafunsa Mulungu
1.248687
Yesu alefwaya ukubapeela umulimo.
Yesu anali ndi ntchito yoti awapatse.
1.24865
"Kashā Kekwaikele Muntu Unena Nabya"
"Nthaŵi Yonse Palibe Munthu Analankhula Chotero"
1.248612
Jon: Bwisambila pa bulopwe.
Jon: Lembali lanenanso za ufumu.
1.248492
Nansha le wiivwananga na mweivwanine Ed?
Kapena mumamvela monga mmene Ed anamvelela?
1.24836
Mu bipangwa byonso bya Leza, mikōko yādi imweka bu isakilwa bukwashi kutabuka, enka na ayo yāpangilwe mwanda wa kwikale muntu wa kwiyendeja ne kwiilama.
Pa zolengedwa zonse, nkhosa zinkaoneka kuti sizingayende zokha koma zinkafunika munthu woti azizitsogolera komanso kuziteteza.
1.248312
Bushe Kwaliba Uwingeshiba Ifya ku Ntanshi?
Kodi Pali Amene Angadziwiretu za M'tsogolo?
1.248109
Inya, panuma ya kufumyapo ukubifya konse ne bantu imbifi pa calo.
Inde, atachotsera dziko kuipa konse ndi anthu oipa.
1.248101
Kabili Sekaria pakumona alisakamikwe, no mwenso walimwikete.
Ndipo Zakariya anadabwa pamene anamuona, ndipo mantha anamgwira.
1.248029
Nga kanshi nashuka shani ica kuti nyina wa kwa Shikulu ese kuli ine?
Zatheka bwanji kuti mayi wa Mbuye wanga abwere kwa ine?
1.248026
Kani abantu abengi balabona shani imilimo bapyunga?
Kodi anthu ambiri amaona bwanji ntchito yawo?
1.247962
Kabalabila ati: "Mukabeshibila ku fisepo fyabo."
Iye anati: "Mudzawazindikira ndi zipatso zawo."
1.247954
Bushe Kwaliba Uwingeshiba Ifya ku Ntanshi?
Kodi Pali Amene Angadziwiretu Zam'tsogolo?
1.247944
Ico cipusho calyaswikwe mu 1931.
Funso limeneli linayankhidwa m'chaka cha 1931.
1.247921
E ico bamwipwishe abati: "Itempele ili lyakuulilwe mu myaka 46, bushe iwe ukalimya mu nshiku shitatu?"
Pamenepo Ayuda anati, Kachisi uyu anamangidwa zaka 46, ndipo kodi inu mudzamuutsa masiku atatu?
1.247913
Kupwa, twesonga mu Kenya.
Kenako tinakwatirana ku Kenya.
1.247862
Umu 1980 yatutumile uku Nigeria.
Mu 1980 tinatumizidwa ku Nigeria.
1.247763
Abebele ati: 'Mwikafuma mu Yerusalemu.
Anawauza kuti: 'Musachoke mu Yerusalemu.
1.247579
Paaleni Ukulongana Kwesu 94.
Dalitsani Misonkhano Yathu 94.
1.247529
Le Tufwaninwe Kutyina Satana?
Kodi Satana Tizimuopa?
1.247214
3 Naashi tave shi mu ningile, osheshi inava shiiva Tate, vo kave shii nge.
3Iwo adzachita zoterozo chifukwa sanadziwe Atate kapena Inenso.
1.247201
Lelo ici cacitike pa kuti twi-icetekela fwe bene, lelo tucetekele Lesa uubuusha abafwa.
Zinatero kuti tisakhale ndi chikhulupiriro mwa ife tokha, koma mwa Mulungu amene amaukitsa akufa.
1.247173
Ukulongana kwa muputule ukwa kubalilapo uko twasangilweko mu El Salvador
Msonkhano wathu woyamba ku El Salvador
1.24709
E lyo abepwishe ati: "Bushe uyu umutwe ne fi balembapo fya kwa nani?"
Ndiyeno anawafunsa kuti: "Kodi nkhope iyi ndi mawu akewa n'zandani?"
1.246795
I vyani vino kasema umwi wino atalumbulwa uwafumile ku Yuda wafizilwe ukucita, nupya icani cafumilemo?
Kodi n'kuphonya kuponi komwe mpolofeta wa ku Juda adacita, ndipo n'ciyani comwe cidadzacitika?
1.246683
Ee, naliimwena no kushininkisha ukuti, uyu e Mwana wakwa Lesa."
Penepo ine ndaona, pontho ndisacita umboni kuti uyu ndiyedi Mwana wa Mulungu."
1.246638
Awe, na Yobo wine te fyo atontonkenye.
Ayi, ndipo nayenso Yobu sanaganize choncho.
1.246628
Lyene Mose uumile umu ciliwe imiku iili, na manzi aingi yatandika ukufuma.
Ndiyeno Mose akumenya thanthwe'lo kawiri ndi ndodo, ndipo madzi ochuluka anatulukamo.
1.246424
(Pantu ifi fyonse e fyo Abena fyalo bafwaya).
Pakuti anthu a mitundu ina akufunafuna mwakhama zinthu zonsezi.
1.246326
Kabili ici e cishibilo muleishibilako: Mulesanga akanya nabakapomba mu nsalu kabili nakalaala mu ca kuliilamo ifitekwa."
Ndipo ichi ndi chizindikiro kwa inu: mudzapeza mwana wakhanda wokuta ndi nsalu atagona modyera.
1.246294
10 Inte cine cine balasakamana abantu.
10 Mboni zimasamaladi anthu.
1.246282
Mulefwaya Ubufumu, Mwilafwaya Ifyuma
Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina
1.24625
Bamama abafyele bamayo basambilile icine mu 1908.
Mayi awo a mayi angawa anaphunzira choonadi mu 1908.
1.246151
Lelo, bafwile 'ukulaikala ifi fine na bakashi babo ukulingana no kwishiba.'
M'malomwake ayenera 'kupitiriza kukhala ndi akazi awo mowadziwa bwino [kapena kuti mowaganizira ndi kuwamvetsa].'
1.246073
(Ku ca kumwenako, bushe ulomfwana bwino na bantu bambi?
(Mwachitsanzo, kodi mumacheza bwino ndi anthu?
1.246073
(Ku ca kumwenako, bushe ulomfwana bwino na bantu bambi?
(Mwachitsanzo, kodi mumacheza bwino ndi anthu?
1.245996
Nalyasukile ati, "Nshishibilepo uuli onse uwikala ku China."
Ndinamuuza kuti: "Sindidziwa munthu aliyense ku China."
1.245937
Bamwaswike abati: 'Twalitiinine!
Iwo anayankha kuti: 'Timaopa.
1.245872
Bushe Mulakwata "Ifya Kulya pa Nshita Yalinga"?
Kodi Mukulandira "Chakudya pa Nthawi Yoyenera?"
1.245868
Wa nsansa umuntunse uucita ifi."
Wodala ndi munthu amene amachita zimenezi."
1.24572
Pamo bwa batumibwa, netu tusapulanga ku njibo ne njibo.
Mofanana ndi atumwi, timalalikila nyumba ndi nyumba.
1.245667
Ne Nshiishi yalemukonka pa numa.
Ndipo Manda anali kumutsatila pafupi kwambili.
1.245486
10 Nomba cinshi Maria aali no kucita?
10 Kodi pamenepa Mariya akanatani?
1.245475
Mfulo mfulō, 'bakokwa ne kongolwa na bya kusakasaka bya abo bene.'
Iwo 'amakopedwa ndi kukodwa m'chilakolako chawo.'
1.245221
Amafya ya mu bushiku bumo yalilinga kuli ubo bwine bushiku.'
Nsiku iri-yense imbakwane na bzakuipa bzace.'
1.245216
Pakuti icikonkoli canji ciliweme; icipinto canji cilipubile."
Pakuti goli langa ndi losavuta ndipo katundu wanga ndi wopepuka."
1.245111
20 Ifyo twingacita pa kuti tube ne citetekelo nga Yobo.
20 Kodi tingakhale tani na cikhulupiro ninga ca Djobi?
1.245015
Ine, ne Yehova, nkacilenga ukucitika bwangu bwangu mu nshita ya ciko."
Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake."
1.244945
Na Angela mu 1975, kumeso kwa betwipangule ku televijo
Ndili ndi Angela mu 1975 tikudikira kuti atifunse mafunso pa TV
1.244911
Baibolo ilanda ukuti pa nshita shimo bamalaika balecingilila bakapepa ba kwa Lesa aba cine pa kuti bafikilishe ukufwaya kwa kwa Lesa.
Baibulo limasonyeza kuti nthawi zina angelo amateteza anthu okhulupirika pofuna kukwaniritsa cholinga cha Mulungu.
1.244897
"Mukamona . . . apalekanina umulungami no mubifi." - MAL.
"Mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa." - MAL.
1.244785
Pamo bwa batumibwa, netu tusapulanga ku njibo ne njibo.
Mofanana ndi zimene atumwi ankachita, ifenso timalalikira kunyumba ndi nyumba.
1.24468
6 Ukupeela u kusuma sana.
6 Kupereka zinthu kumatithandiza.
1.244658
Batumoni bakankamane ba mu Danemarke mu myaka ya 1930
Mboni zolimba mtima za ku Denmark m'zaka za m'ma 1930
1.244611
Bushe tamulembona?
Kodi simukuona?"
1.244599
4Uko ndeya, inshila mwaliishiba."
4Inu mukudziwa njira ya kumene Ine ndikupita."
1.244468
Ni bani bakonaula ukupepa kwa bufi?
Kodi ndani adzawononga zipembedzo zonyenga?
1.244444
Ca cine, nalishiba ukuti lyonse mulang'umfwa."
Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse."
1.244224
Twikankamikei Batwe Bene na Bene, 'Nakampata Pano Po Pene'
Tizilimbikitsana Ndipo "Tiwonjezere Kuchita Zimenezi"
1.24422
" Bene bakakuula amayanda, no kwikala muli yene (abene beka); kabili bene bakalima amabala ya myangashi no kulya ifisabo fyaiko.
Iwo [anthu okhala m'dziko latsopano limene Mulungu walonjeza] adzamanga nyumba ndi kukhalamo; ndipo iwo adzawoka minda yamphesa, ndi kudya zipatso zake.
1.24422
" Bene bakakuula amayanda, no kwikala muli yene (abene beka); kabili bene bakalima amabala ya myangashi no kulya ifisabo fyaiko.
Iwo [anthu okhala m'dziko latsopano limene Mulungu walonjeza] adzamanga nyumba ndi kukhalamo; ndipo iwo adzawoka minda yamphesa, ndi kudya zipatso zake.
1.244087
Babatangilila mu kasuba ne kumbi, kabili mu busiku babatangilila ne mulilo.
Akhawatsogolera masikati na mtambo, ndipo usiku na ceza ca moto.
1.244034
Osheshi eshi ashishe ovapaani tave shi kongo.
Pakuti anthu a mitundu ina akufunafuna mwakhama zinthu zonsezi.
1.243991
Imwe munjita ati, 'Kasambilisha,' kabili, 'Shikulu,' ico cena mulalungika, pantu e fyo naba.
Inu mumanditcha kuti 'Mphunzitsi' ndi 'Ambuye,' mumalondola, pakuti ndinedi.
1.243838
(Tala efano pehovelo loshitukulwa.) (b) Omolwashike Moses a li a hoolola okuhepekwa pamwe noshiwana shaKalunga?
(Onani chithunzi pamwambapa.) (b) N'chifukwa chiyani Mose anasankha kuvutikira limodzi ndi anthu a Mulungu?
1.243826
I kitatyi'ka kyotwalombele dya mfulo kya pamo ami ne mwinē pami?
Kodi ndi liti pamene ineyo ndi mwamuna kapena mkazi wanga tinapemphera limodzi?
1.243786
Elyo abasambi bakwe batile, Kasambilisha, nga nalala ali nokubuuka.
Pamenepo ophunzirawo anati: 'Ambuye, ngati iye akupumula, apeza bwino.'
1.24378
24 Pādi kwishila na Kena.
24 Koma zinali zosiyana ndi Kaini.
1.243779
Tulacingilila Imitima Yesu 37.
Titeteze Mitima Yathu 37.
1.243574
Davidi alikwete fyonse ifi twalandapo; lelo lyonse ali uwaicefya.
Dhavidhi akhali na pinthu pyenepi pyonsene, mbwenye iye akhali wakucepeseka mu umaso wace onsene.
1.243569
Kabili aisa kuno mu kofwa Paulu.
Ndipo iye adabwera kumweko kudzathandiza Paulo.
1.243402
Byo mumwenamo: Lesa wimulaya kwimupa bumi bwa myaka ne myaka inge mwamuyuka.
Chimene chili kwa Allah, ndicho chabwino kwa inu ngati mukudziwa.
1.243371
Mose na bena Israele balishibe kale ishina lya kwa Lesa.
Mose na Aisraele akhadziwa mwadidi dzina ya Mulungu.
1.243338
"Kukekala lusanguko lwa baoloka ne babula koloka."
"Kunadzaoneka kulamuswa muli akufa kwa anthu akulungama na akukhonda kulungama."
1.243271
Kādipo ubwanya kufuta lupeto'lwa ponka na ponka.
Sakanatha kubweza ndalamazo nthaŵi yomweyo.
1.243169
Linda: Ine na Sally tatwaishibene pa myaka ukucila pali 20.
Linda: Ine ndi Sally sitinkadziwana kwa zaka 20.
1.243131
Natonge umo mu bandi bana bu mulopwe.'
Ndasankha mmodzi wa ana ake kukhala mfumu.'
1.24311
22 Lelo abo i Bahebelu?
22 Kodi iwo ndi Aheberi?
1.243074
12 Tungasambilila ivintu ivingi sana uku mapepo aalembwa muli Baibo.
12 Tingaphunzire zambiri pa mapemphero amene analembedwa m'Baibulo.
1.242734
Inoko, i kutupu nansha umo ukapona pa nshi Shenu kuyuka mpika. . . .
Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa. . . .
1.242523
6 Shi tūminine tukapalwa mpalo.
6 Ifenso tikapirira tidzalandira mphoto.
1.242386
Bushe tamwaishiba ukuti mfwile ukuba mu ng'anda ya kwa Tata?" - Luka 2:49.
Imwe nkhabe dziwa kuti ndisafunika kukhala n'nyumba mwa Babanga?' - Luka 2:49.
1.242261
"Kabili bakakuula amayanda no kwikalamo; bakalima na mabala ya myangashi no kulya ifisabo fya yako.
Iwo [anthu okhala m'dziko latsopano limene Mulungu walonjeza] adzamanga nyumba ndi kukhalamo; ndipo iwo adzawoka minda yamphesa, ndi kudya zipatso zake.
1.242241
Ku ca kumwenako, tontonkanya pa myeshi 6 iyapita.
Mwachitsanzo, taganizirani zimene mwachita pa miyezi 6 yapitayi.
1.242131
Kabili Mose alabila ati: 'Uuli onse tekusyapo imbi mana ukufika akasuba kakonkapo.'
Ndiponso Mose awauza kuti: 'Munthu aliyense asasiyeko mana akuti akadye tsiku lotsatila.'
1.241912
Le kemwadipo muyukile amba mfwaninwe kwikala mu njibo ya Tata?" - Luka 2:49.
Imwe nkhabe dziwa kuti ndisafunika kukhala n'nyumba mwa Babanga?' - Luka 2:49.
1.241807
Nalitemenwe Sana Ubwangalo bwa Baseball!
N'nali Kukonda Baseball Kuposa Cina Ciliconse
1.241763
Bushe Mulamona "Uushimoneka"? _ Ulwa Kusambililamo
Kodi 'Mukuona Wosaonekayo'?
1.241662
Tabaumfwile ifyo Noa alebasoka.
Anthu ananyalanyaza zimene Nowa anawachenjeza
1.241622
Naleikala na bamayo na bakalamba bandi abanakashi batatu.
Ndinkakhala ndi mayi anga komanso azichemwali anga atatu.